Malawians arrested in South Africa after truck crash
Two Malawian nationals were arrested on suspicion of stealing goods worth R65 000 after the truck they had been driving crashed on Saturday.
Western Cape police spokesman Inspector Lindikhaya Mkhontwana said the two men were transporting computers, motor boat engines, television sets, electronic appliances, bicycles, music systems and bank notes when the incident happened.
“The pair could not provide police with proof of purchase and transportation documents.”
They told police the items were being taken to a Johannesburg terminal to be transported to Malawi.
Mkhontwana did not provide details on how the accident occurred.
Both men
are expected to appear in the Laingsburg Magistrate’s Court on charges of being in possession of suspected stolen goods on Monday. – Sapa








Kufuna kuonetsa kuti kuli tight security with the recent games that are to take place in south africa.Mbava zambirimbiri mu Khayelitha umu,hillbrow,soweto azikalambana ndi amalawi apa.
palibe nkhani apa. A Malawi timanyamula katundu opanda ma documents nthawi zonse. Monga a ntchona a kwanu akandipasira katundu kuti ndidzapatse inu osauka ku malawi ndikane chufukwa palibe ma purchasing receipt? Aaaaaaaa.
They were supposed to have papers for the goods.Ngati atumidwa ndiye angofera za eni
Ingonenani za ngozizi basi. Kuli ma transporter ambiri amene amatenga katundu ku RSA kupita naye ku malawi, ndipo wambiri mwa katundu ameneyi sakhala ndi mapepala, lero lokhalokha kuwagwira zatani. Katundu ameneyo sakhala wa munthu m’modzi ayi, ndipo ambiri amangopatsidwa ndi mabwana awo.
Nkhani palibe apa yakula ndi nsanje. Ngati akufuna mbava apite ku nyanga, khayelisha, khayamandi, kumene anthu sadikira kuti kude pakubera anthu.
Asiyeni ma transporter awo katundu siwawo.
SORRY GUYS!!! NEXT TIME WHEN U BUY GOODS REMEMBER TO KEEP RECEIPTS, PAJA NDINU ACHAWA FROM MANGOCHI UMBULI, NEXT TIME PLZ REMEMBER TO KEEP RECEIPTS. SORRY GUYS.
nchawa nde ndani? iwenso mbalame eti? ndiwenso mbuli coz eva since u started learning about tribes in primary xool dere z no tribe as chawa.if it z 2 b found, den i gues ndi mtundu wa ambuyako.mphawi iwe nsaje basi.
In this modern ignorant malawi,you are best known by your tribe and where you come from,than being a malawian.Thus the description of democracy by Mlakho.
Really,we have gone back to square one.We thought that we have moved forward but that not the case of the everyday division by our old tyrant.Kaya tione mmene zithere.
Komatu iwe tinenenji Maluwa uzimangiliratu.Nchawa modzi wapezeka koma simuti mumwe tameki zomwezi.Pamene pakufunika cross breed btwn Mchawa and Mlakho to smoothen things in nyasaland.
achawa ndiye kuti chiyani? zili mubuku liti zimenezo lomwe iwe unawerenga? tawerenga mabuku ambiri koma sitina pezepo liwu loti achawa mbulinondiwe siunawerenge mabuku ambiri. bwera pa 27 march pano uwone ayao akulandira madiploma ndi ma degree ku domasi college
Muyao,kaya mchawa ntchito yake imene amadziwa ndi bizimisi.Sukulu wayidziwa liti nchawa?
Sanu mukalindira zitupa za diploma ndi Domasi.Really a way forward for Mchawa.
Nthawi zina kunyozedwa kumakupangitsa kulimbikira.Look now you are going to get diplomas and degrees very soon.
first of all 3Degrees should be sorry for himself for his childish thinking. Which district in Malawi are you coming from? I wonder if you are a Malawian at all, you dont even know that Malawi is sold becoz of Mangochi worldwide SHAME!!!!!
Akuba awa. Amangeni basi. Iyaa. Amalawi ena mukumapita ku Joni kukachita uchifwamba ndi using’anga waboza. Kumabera mabuno kumeneko mukabwera kumudzi muzidzaphoza ngati katundu munakhetsera thukuta ali wakuba. Azikugwirani choncho mwina mungasinthe. I remember late businessman in Bangwe who used to go to RSA with fake mandrax. Mabuno atamutulukira anakamugwira ku Maputo ndikumudula miyendo ndi mikono kwao ndikumugulira wheel chair kenako kumukweza ndege back to Malawi. Amalawi enanso mukumapangana chiwembu nokhanokha. Manyazi mulibe eti?
IT IS SAID KWAENI KULIBE MKUWE GUYS, MWAONJEZATU KANDU OPANDA ZIPHATSO NGAKHALE KU MALAWI AMALANDA KOMANSO KUMANGA MUNTHUYO.
it ashame that most people post there comments on nyasa net without doing any invistigations.im one of the victim.isend my mami apc,fidge&5000ZAR CASH,all of my belongings had papers.im just wishing them aquick release&im ready to testify in the court that those guys didnt steal those goods.
Ndi akuba kulikonse katundu wopanda mapepala apolisi amati ndi obedwa, Achawa akuchitisa manyazi dziko la Malawi, sukulu inakupitani kumanzere, ntchito zanu nzosaziwika bwino, mumabwera kuno opanda ma Passport, magalimoto ambiri kuMangochi ndiopanda misonkho, ma namba plate a joburg, kukana kusintha (umbuli). Kunyamula katundu wopanda mapepala mapeto ake ndi zomwezo. Electronix are very sensitive items . Fridge, computer, HI-fi ,how did u pay customs if at all u did? Kuzolowera ziphuphu kwa apolisi, muzachangamuka liti aChawa ndi Jubeki ino…
UHHH THOSE GOODS HAVE PAPERS KOMA APOLICE AKUNO ANGOFUNA KUWABELA ANTHUWO COZ THERE FOREGNERS,APOLICE AKUNO NDIWO MBALA NUMBER ONE AKAONA NDALAMA NTIMA WAO SUKHALA MMALO.THOSE PEOPLE ARE TRANSPOTERS THEY CANT CARRY GOODS WITHOUT PAPERS, SO MIND U WEN MAKING SILLY COMMENTS.