Email a copy of 'Ndanga tips Malawi cabinet on communication strategies' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chitsa boys
chitsa boys
8 years ago

Zanu izo a mcp ife tikudikila project kwa kammwamba ndi kwa kameza inu zitukwanani kuchoka pa phalula kupita kwa kammwamba mdi k200. Min bus tipeza mwai wa ntchito inu muli choncho

botomani
botomani
8 years ago

Just pass on your tips to BABY Mulizi and you will be lest assured that government will receive them. Don’t waste our time !!! Mwanva ?

Mr Dowa
Mr Dowa
8 years ago

Mr Ndanga mwalankhulako zonveka, komano dziwani ichi zomwe mwalankhulazo ndichifukwa choti azanu a Opposition alankhula ndi mtima wonse kuti Boma silidachite bwino pa nkhani yotenga anthu ambiri, zomwe zikonetsa kuti ndalama za Boma zaonongedwa zambiri,choncho my free advise kwa inu ndi awa,Dziwani kuti ndi chisankho chomwe chinapangisa kuti kukhale Opposition ndipo Boma ili kukanakhala kuti kulibe chipani cholimba ngati MCP osati zanuzotu kikkkkk panopo tikanakhala tikukamba zoti dziko Malawi latha chifukwa palibe chanzeru chomwe chikuchitika,Mukudziwa inu kuti Boma la Democracy limayenda bwino pakakhala Opposition yamphavu?Tiyerekeze kuti UDF yanuyo ndiyo ya Opposition zikanakhala bwaaaaaaaaaaaaaaa?

Noxy
8 years ago

Brilliant Ndanga keep it up!

mhango
mhango
8 years ago

Keep it up ndanga,, its tym to develop the country,,nothing wrong working wt government it happens any where,, please kumaenda u LL know more,, suzingotukana bona daily nooooo,, Atupele is udf president n udf is strong,,

mhango
mhango
8 years ago

Mo fire UDF, ndanga keep it up,, osamvela enawa ama jealous,, udf as strong party must advice wen necessary,,what others want is nkumangotuka not advising ,, those hu think udf is not strong u r making a mistake,, udf ilipo n strong ,,more fire udf..keep working wt government,its tym to develop the country not kumamgolongolola ,,,

Tili Chenene
Tili Chenene
8 years ago

UDF, be quiet

Blunt Truth
Blunt Truth
8 years ago

It is painfully obvious that Ndanga has never worked in govt. No minister can publicly speak about govt matters without the president approving. The fact that the list of 106 people taken to New York has not yet been released means Peter Mutharika has not approved that it be released. These ministers were told to say what they said and they cannot dare say anything beyond what they were told to say. That is why they were uttering the nonsense that DPP inherited the mess from PP when the truth is that Peter Mutharika is failing.

mbuli zophunzila
8 years ago

Ka UDFnso. Nkachani,mwalephela kuyendetsa kachipani ndie mwati mulangize cabinet? Ha ha ha wonders shall never end!!!!!!!!!!!!!!!!

Read previous post:
Breast cancer month, do something to give hope

Surely in today’s world, everyone will be touched by cancer as a patient, a family member or a friend; unfortunately...

Close