Email a copy of 'Newly married Ben Phiri and Twamie 'happiest couple’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Newly married Ben Phiri and Twamie 'happiest couple’' to a friend
President Arthur Peter Mutharika says the strengthening of Malawi-China ties over the years has been a double edged sword which...
How old is Ben Phiri, hi Dr? How old is Twammie? Is she the 1st wife? Where was the receiption? Kukwatira mamuna ndi mkazi ndikofunikadi eti? Kodi paja anachoka pa special one? Kuiwonera patali
Kodi ma church nowadays akulola mitala? last week there was also another wedding officiated at St Columba but I understand mkazi ameneyo ndi wachitatu if not four, what is the church trying to tell us? kodi malamulo anasintha? Akhrstu chimene tikuchita sitikuchidziwa ndithu!
Third…? enao anatisiya else there were no “till death does us part” vows?
Conglatulations Ben and Twammie. Keep it burning! Keep the promise.
Kodi zomaphikira mamuna zinakalipobe, Siaka..? Masiku ano banja is partnership rather a union to oppress women’s ambition to work, do business or study. Mkazi ntchito yake sikuphikira mamuna ayi, nzachikale zimenezo.
Ali ndi mwayi mkazi koma funso nali”akuziwa chifukwa chomwe mnzawo anachokera”?
Rubbish reporting nyasatimes.These days you are no longer objective always sucking up to some individuals whether its bushiri or Ben Phiri whilst trashing other people for nothing. For one why can’t you tell people that this is the third marriage for Ben Phiri or the huge age gap between them. Cheap tabloid!
bwana BEN! timati tipemphe nawo! tilembeni tchito yokolopa ndi kuphika nanga madam wo angakolope amenewo? angaphike? coz ndi golidetu golide!
congratulations Big man
Kachitatu aPhiri kukwatira, i hope awa ndi mapeto. Good luck to both of you