Email a copy of 'No politics at Kulamba ceremony for Chewa people' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'No politics at Kulamba ceremony for Chewa people' to a friend
Since taking office following the highly contested and controversial polls last year, President Peter Mutharika has spent a high amount...
A Lomwe Amapita Kukakumbutsana Ndikulimbikitsana Pa Zachikhalidwe Chao Ngati Alomwe Samapita Kukalamba Munthu.Leave Mlakho For Lhomwes And Kulamba For U.Palibe Mu Lhomwe Yemwe Amakhumbira Kapena Nditi Kulakalaka Kukhala Mchewa Sindikukhulupiliranso Kuti Alipo Mchewa Yemwe Amafuna Kukhala Mu Lhomwe.A Lhomwe Alibe Nazo Ntchito Za Kulamba Sizikuwakhuza Chirichonse.Ur Organisers R Not The Mulakho Organisers.Pangani Zanu Musamaphulike Mkabudula Ndi Mtundu Wa Amzanu.
Kkkkkkkk shame Mlakho wa Angulu
Good culture place rules not the copied culture like !!
Alomwe should learn this.
Thumbs up wena tenganipo phunziro
Kodi alomwe mulibe supreme leaders eti? That is why you act like wild dogs.
Ngati Ndife Amozi ,mfumu Imodzi ,why Tikumathamangitsana Mmaiko,ndipo A Gawa Akuchitapo Chani?Zikhalidwe Zizindikire Kuti Zili Ndi Udindo Okweza Maiko Athu.Tisamangoononga Ndalama Muzikhalidwe Pamene Abale Akusowa Ndi Ya Machesi.Ma Project Ali Phwi Mmaiko Koma Kusakaza Ndalama In The So Cod Culture,
Thats gud mr organizer politics not gud in the evets like this me as a chewa I am comfortable with the distion
Mwamva inu Alakho????!! I am sure even alomwe a serious dint want to be part of ulakho because they support other political parties and ulakho = udiphiphi (kodi a Ntaba alipo by the way?) Its too late to depoliticise ulakho .. Bravo Achewa!!!
I was surprised oneday in France i met a guy from CONGO who told me his name was GAYIRENI MASAMBA.
I Asked are you from MALAWI ??
HE SAID NO; WHY??His name sounded more like chewa you know ??
I THINK THERE ARE STILL SOME CHEWAS REMAINING THERE !! I CONCLUDED TO MYSELF !!
HI