Email a copy of 'Nomads, BB Carlsberg final grosses record K29 million' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads, BB Carlsberg final grosses record K29 million' to a friend
Famous Nigerian stand-up comedian Bright Okpocha, better known as Basketmouth, will be coming to perform in Malawi later this year. The...
wa mkaka tikadamwa ife a noma
Vula ikagwa kumachuluka zoliralra
Pepa nebaaaa ! Kkkk
Iwe mbuzi eti nde unamva kuti commentator sakhala ndi team yosapota? Ukati unene kuti mma radio station akunena zoku ti Noma yabelekedwa, Agalu inu munajaila kukoza osagwirira mmaona ngati muzingowina yakuwawani hvy iyiyi. Forgt about this ASAP otherwise u gonna luz ua super league form mukalimbana ndi zammbuyo
Y hiring an expatriate ref,noma never looses in finals
Nyerere ndi fire!!!
Neba, mwaluza basi osatha mau. Dzulo lina lanu mu Tnm. Lero ndi lathu mu Carlsberg Cup. Dzanja lalemba basi, 2003 munatibera panonso mumafuna mutiberenso??? Neba, pepani kuti maliro anali onyamula tinayenera kukhala nawo koma kunatalika.
I think ma referees should come from media houses. it looks most of us believe media houses on soccer pitch decisions than the referees.
Who is closer to the players between the ref and the media? The best media can do is to show whether the ref made a wrong decision or not, but we cannot bank on what they say. Let them show us. Otherwise Congrats to Nyelele. BB there is always next time.
Vuto si ife a BB koma ref. wokondera denying us penalty ngati unaguidwa ndi Yona ndalama zimenezo suzimva kukoma. Everyone even different commentators from various media houses saw it as a penalty iwe wekha sunaone bwanji? ufiti chani?
kkkkk bullets kuwina koma mpirao mumkaoneradi inuo..Noma woyeeeeeeeeeeeeee