Email a copy of 'Nomads eye double cup glory: Standard Bank Cup fixtures out' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads eye double cup glory: Standard Bank Cup fixtures out' to a friend
One of the activists pushing for federal system of government, Dr Binnah Shawa has called on President Peter Mutharika to...
B4ward woyeeeee std cup tiphula bas
Mavendor amvutlapo kt avomeleze komabe cup tatenga bax
There are reasons records are kept, one that they speak for themselves
Wina afune asafune Noma ndimoto
Aganyufe we gonna b waiting results only, prior 4rm matimu ovoteredwawo. Mpaka thru vote? Which means dey r not gud enough to compete in STD Bank? Kkkkkkkkk koma abale zili kumudzi, muzitiuza results!
Noma ndi motooooooooooooooooooooo!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Thanx redeem for your comment, Palibe munthu oti ine ndine aliyense azivomereza osamangokamba zambirimbiri chifukwa choti wangoja kuzipopa bwanji?
Koma ndiye mulira chaka chonse. Kumayenda kumaona agalu a michombo kuzolowera pa Kamuzu Stadium kumangobelekedwa ndi ma ref for fear of being beaten game ya MAFCO munkaluza 1-0 ref gave you a dubious penalty mwazina lero.
Mpira unatha Ku Malawi kalekale. Idzi masanje eni eni bola kuonela English league.
BOLA ZITSIRU ZAKU FAM ZIKUPATSESONI REFREE WOGULITSA MAJUMBO UJA KOMA KUPANDA KUTERO IWALANI ZIMENEZO NDIMALOTO ACHUMBA AMENEWO