Email a copy of 'Nomads GS tells supporters to provide financial support' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads GS tells supporters to provide financial support' to a friend
Lilongwe Magistrate Court has found Malawi Congress Party (MCP) deputy director of youth Wyson Zinyemba Soko guilty of theft and...
Butao Noma yathu tinayesa kulowa koma there is no response, i tried 3 times kenako ndinasiya
i thot JB gave u K25 mil..y ddnt u invest tht money…th team is performin poorly az wel so thrz no motive 4 th supporters 2 donate funds
BUTAO YOU ARE RIGHT. A GENUINE NOMAD CANNOT TALK RUBBISH ABOUT HIS CLUB. TEAMS EVERYWHERE ARE SUPPORTED BY THEIR FANS. IN CASE YOU DIDN’T KNOW, A SUPPORTER SUPPORTS THE CLUB WHILE A FAN IS A CHEER LEADER. BWITOTO, EDWIN,NEWX AKOKO, MBOLO SIDWALA, NONSENU PAMTUMBO PANU SIINU A MANOMA ZITSILU, MUKANAKHALA PAFUPI NDI KANAKUPATSANI MAKOFI.
Be original in your plans of findng money 4 the club, zokopera sizikuthandizani!
Zausilu zimenezo muchoke nonse kumeneko. Tikufuna kanyenda abwele kumeneko
Team sikuchita bwino ndiye choti tizionongela ndalama ndi chani? Bola ikanati ikumawina ma game bwenzi tikuyesesa. Koma tangosanduka chitonzo kwa anthu. Zimatipweteka
Koma ndiye eeee,ochemeleradi enieni. Ndiye mwati azithandidza timu ndi ndalama? Chaka chino tiberedwadi nkhopezokha zikulankhula kuti ndi mbava zenizeni.