Email a copy of 'Nomads lose preseason friendly to Red Lions' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

19 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Estess Msaka
Estess Msaka
9 years ago

Noma takunyadilani olo taluza 4-3. Iyi ndi friendly kusiana ndi zinazi.

Ashraph
9 years ago

Ya silver yokhayo kuzangoluza tizagenda

fisher
fisher
9 years ago

Anyerere mwakumana ndimikango yakuZomba mumayenda mbali

fodya
fodya
9 years ago

congrants ma reds , GOALS GATE IN SUDAN as ALHLY TEACH A LESSON KWA ANA OSASAMBA

njolomachipilingu
njolomachipilingu
9 years ago

Neba imeneyi timati certificate of attendance.Basi mwachita attend mpikisano kazibwerani.Nomads coaching panel please wise up and polish everything in readiness for the season.You have everything at your dispossal.No exchuses this time sitiyimva yama tchuzi

Ngwazi D
Ngwazi D
9 years ago

Bullets yaluza, Noma yaluza palibe kuti awa aluza kwambiri kuposa anzawo.

Mzimba Solola
Mzimba Solola
9 years ago

Thats good, Kanannji & your backroom staff ntchito ndi imeneyo tsopano. Try also other teams kuti muoneretu mavuto onse. Congrats Reds!

Zinja
Zinja
9 years ago

bola ma noma nanga ndi ndizaku sudan taona dzulo malodza enieni zibwerani mwatuluka basi kkkkkkkkkkkkk

Shoes
9 years ago

Report wapanga improve kalembedwe kwambiri..keep it up. Osati zizungu timaziona apa…

Pappa
Pappa
9 years ago

Tikhala bwino osadanda

Read previous post:
Bullets hammered 0-4 in Sudan: Coach believes Malawi champions can overcome deficit in BT

Malawi champions Big Bullets on Sunday suffered a humiliating 0-4 defeat to Sudan’s Al Hilal in a 2015 Caf Champions...

Close