Email a copy of 'Nomads subdue Chilumba uprising to avoid Carlsberg Cup upset' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nomads subdue Chilumba uprising to avoid Carlsberg Cup upset' to a friend
Peoples Party (PP) Secretary General y Ibrahim Matola is receiving death threats from anonymous elements following President Peter Mutharika’s public...
Bola zaenda basi osachulutsa zonena ai.
Bola tinawina enawo pakamwa ndi pawo.
Chi team chakawawa koma Mighty Beforward Wanderers ….. beside kuwina zigoli zambiri komanso excitement yapa ground izikhalapo sizomwe ikumamenya Bullets za zii.
Noma nde imeneyo… We r moving forwad monga ife mawanders
sitizatengera zigolri man kuwina ndi kuwina basi
Chachikulu bola tawina enawa akanatimvesa kuwawa.noma for ever.
the most important thing is dat we are thru…..but we need to beef up the squad
koma kukondera kwinaku. Pang’onong’ono tikanawina gemyi.
Plz panel ya2,esesan kugula ma strikers abwino.Tatopa ndkunyozedwa ife mseumu mwava.#Chigoli chmoz bac
Guys kip it up, fire fire fire second round tiwine ma game onse guys. Bulletstu chiukepo akupita ndiye sadziwinanso. Mapopa kaunda u deserve extra salaray just give me ur account number zikuponyerako kangachepe wamva? Mapopa iweyo ukundimvetsa sugar kapena suga sekeseke kuyoyopera