Email a copy of 'Nomads to trim squad -Chamangwana' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

7 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
devilsadvocate
devilsadvocate
8 years ago

70 yogulira nyagwita ndikupanganso perform badly mungopita Ku chipiku league. Norma ili ngati an illiterate woman married to a rich husband something’s will neva change. Nena tamapita Ku sukulu ya kwacha ukachotse umbatama. Ngakhale akuti reserve ndiye kumangogula ndi nyagwita zomwe? Mupange ubale ndi Chief’s Ku jozi. Kodi mkati mwa contract yanu munalibe infrastructure development? When the Jap’s go mudzakhala amasiye ngati m’mene munkamvetsera chisoni muumja

Nijo
Nijo
8 years ago

tinadziwa ife kalionera neba umangomva nde utioneno ife mu 2016 ulira

ziz
ziz
8 years ago

Ku bb umbuli ndi wa mbiri K0:5bn ndiya 5years while nomah K70mn ndi every season, they is no big difference

Nyenyezi
Nyenyezi
8 years ago

I knew it wont work with such a big squad, coach is always confused because he does not know who to pick in first eleven, kaya kunali kutinyadira a BB ife ndiye mwagwa nayo chipepeso chanu ndi Carlsberg mutigwera mutapita kwa AYAYA ku Balakayo, mphoto yake ndi imeneyo kuononga ndalama zogulira wosewera, pa ground nkumakukanikani

WANYERERE
WANYERERE
8 years ago

Jack thats the way to go

Alex Tulama
Alex Tulama
8 years ago

Bola musafe bwino than kuononganso same lyk here Sundowns hv great squard bt their peformans n de squard dosn’t mach.So in my Nyerere camp they hv same mentality eish my be loved NOMAS mwatan kodi?

Gadabwali
Gadabwali
8 years ago

Zataninso nanga neba? Mesa u bought all the star players wth the K70m B-forward sponsorship? Phuma neba, kungoti yapezekeranji sponsorship, kugula maplayer ngati bonya! Mukanakhala kuti mwapeza K0.5billion sponsorship ndye ukanagula maplayer onse a national team!

Read previous post:
Another arrest in fake maize seed syndicate: Lucy Mwitha of Kulima Gold

Police in Dedza have arrested 25 year old woman, Lucy Simengwa Mwitha who works with Kulima Gold shop as Manageress...

Close