Nomads victory parade recap: Pictures as Carlsberg Cup champs turn Malawi blue
Mighty Be Forward Wanderers last week won Carlsberg Cup at the 2015 final match against its rivals Big Bullets by a 2-1 in Lilongwe. The Nomads celebrations last week have been in full flow. Nyasa Times chief photographer Jeromy Kadewere captured photos in the victory parade from Lilongwe to Blantyre.
Follow and Subscribe Nyasa TV :
Ngati chili chimidzi ife tasangalala mchimidzi chathucho koma chimene ndikuona apa ndi nsanje season yachani pamene season ya cup iyi yatha tidzaikambanso next year.
Manoma woyeeeeee! Zakhala bwino.. Inu a BB mmene mumaticinya ife mumatinso ma noma muwacinya? Apo nde ndi woooo
Kkkkkkk,cimizidi eee
timu yaikulu izidziwika, sizachilendo pajatu zimayamba ndi noma,wasanje aphulike bola ndikuva kukoma, makwela kwela muzakwela mphutsi bola kusapota nyerereeeeeeeeeeeeeeeee!!!!!!!!!!!!!!!
Hahaha kodi cup can be celebrated season itatha mesa tournament yake yatha? Why celebrating season itatha while finals yachitika kale? Pepani ngati zakunyasani dikirani nanu nthawi yanu idzakwana. Ngati chiri chimidzi ndiye chimidzi chake ndichokomatu and this was cute, superb, wanderful….. More Fire MANOMA mwatimvetsa kukoma komanso mwatichotsa chitonzo waiting for more of this nature. Wakwiya ndi mfiti. Koma MANOMA aaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa!!!!!! ndidzafe ndidzaole ine?
GABRIEL MWALE OSAYAMIKILA BWANJI CHIMIDZI INU DZIPANGANI ZA KUTAUNI ZANUZO IFE NDI ACHIMIDZI KOMA ZINTHU ZIKUYENDA BASI NDI CHIMIDZI CHATHUCHO
Koma chimidzi chake parading a cup season siinathe eishhhh!!!!
A Gabriel Mwale,what season r u talking about.Ife cup tawina panopa,why should we postpone our celebrations to the end of the season?Malamulo ake ati ndipo chitauni chake chiti inuyo?Ngati zakubowani,bwanji osangokhala chete.Tisiyeni ife eni ake manoma tisangalale mmene tingathele.
Congratulations Manoma, Prepare Another Shelf For Standard Bank Cup.
kanyenda analikonko.