Email a copy of 'Nyasa Bullets budget's K100mil not enough: From rags to riches' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nyasa Bullets budget's K100mil not enough: From rags to riches' to a friend
Sincerely congratulations to Dr. Getrude Hendrina Maseko-Mutharika, Her Excellency the First Lady of the Republic for the award of the...
kuzolowela Kuba ett agalu inu.
This is ”nonsense” and its an insult to sponsors, we had nothing for a good number of yrs, the ”GOOD SAMARITAN” has come in with K100 mln nkumati yachepa. Simukanabwera poyera nkumalankhula zopusazo mukanangozisunga under wrap. Ndakwiya nanuuu.
kuli bwino osayankhula
Kkkkkkk koma zina ukamva handede million so yachepa??????! Hehehe nde mukufuna chani tsopano inu mungapange olo million ndi chenje cha ma memory card?
munasolowela kubazam’mageti agaluinu chifukwasimungalamulile bwanawanu mungofuna tikamakaonela magemu anumusikatipiza m’matumba peyapeya ndimabokosi kumasitandi ndikazakuona ndizakumenyakofi. ??????????
kkkkkkkkkkkkk koma a BULLETS ndi chani? minyama ?
Munazolowera kupemphapempha inu ma vendor ogulitsa ma memory card anyimbo kale. Adani a City
Anthu akuba musatisokonezere sponsorship, zulo tinali PA zero lero 100mita, wena nkumati yachepa, mapulani obera chani?
Timaonangati Tipumakusonkha Koma Mmmm
Mwachita bwino kutidziwitsa thawi yabwino chifukwa anthu akanaona ngat ndalama zabedwa.zinthu zikundula kwambiri kwamunthu oti sanayendetsepo za mpira atha kuona ngat ndindalama zambiri koma eashi ku gopita kukamenya ma away awiri ku mzuzu ndalamaza zambiri.ifendi maule eni eni pavutapo tidzathandizana!!! Kusokha ndiye mkosayamba!!! Ife tilibe problem!!!!!