Email a copy of 'Nyasa Bullets crowned 2015 Malawi football champs: TNM Super League winners' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Nyasa Bullets crowned 2015 Malawi football champs: TNM Super League winners' to a friend
Malawi Human Rights Resources Center (MHRRC) has strongly warned that unless councillors in Chitipa District wake up from their slumber, it...
Chi team icho,Maule ndi Maule baxi sadzathekanso kumwa wa mkaka throughout the whole season its not a joke big up gayz,Nyasa Big Bullets 2016 more fire.
Aliponso wina
thanks Mr Lungu for thanking The Almighty even at better times! Ambiriwa amamfuna Mulungu akakhala m’mavuto basi. But remember that we shall also expect such a brilliant performance come 2016. BB for lyf!!!
At least Bullets yatimvetsa ndi mmene tikulilira ndi Manutdmu. Congrats guys. You really deserved this. You were so consistent and meant business from day one
Ulemu wanu ma bb u deserve it
Bullets ndi ayayayayyayayayyaya
Amene wakwiya ndi BB akakolope nyanja.U Championship ndi umene timawerenga osati zinazi.
Maulle ndi chiteam
ma Ulle omwewo kuti wawawa!!!! Kumwa nawo wa mkaka!!!!
Ma team Nde ndi onse Guys koma Eee bullets nde ndi Ayiyayiya ayiayia ayiayia