Email a copy of 'Omar drags Atupele to court over UDF expulsion' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Omar drags Atupele to court over UDF expulsion' to a friend
Communities in the area of Chief Malemia in Nsanje have turned down a proposal by their traditional leaders to sale...
Ungoyambitsa chako
alomwe youre right some peple amakonda zikamayen da .mabezy .koma.akagwa basi osawoneka.but atupele he dont do that he contienew wark has amalawian leader kip it ap mr tpm we love you
Azibambowa amwa win
Kodi mukamati UDF yatha ngati makatani what do you actually mean? if that is a case why people still fight to be in UDF? that alone signifies to me that UDF is the strong party in Malawi, and Atupele is a good leader. Even though am not UDF but i love Atupele Muluzi, the guy is intelligent and has a good vision for Malawi and he loves his country that’s why after elections he work to save people not like other selfish people.
Kodi banji inu bana Omar sapita pa India kupanga ndale? Ife menye weni weni anaphuna inu panga ndale pa India. Inu alipo siya chabe mana wa Muluzi eh. Banji inu saziwa kuti ali mana amene uja eh. Inu saona kuti mana uja chichi alibe pa mutu kuonesa kuti jeruso alibe eh. Banji inu phuna limbana ndi mana eh.
Kodi UDF ilipobe? Hahahahahahahahhahahahaha! Atupele wachimalizadi chipanichi..
Atupele has his eyes on state presidency as promised to him, therefore come rain or shine he’ll stick with DPP until his ambition to rule is fulfilled.
Kaya kunthanani mutipeza.
Atupele ndi munthu ozikonda kwambili ndi bambo ake omwe sianthu abwino kuno ku mangochi anangwiritsa anthu ntchito lero oro kwa uza kuti zili pati tizapezana 2019 nanga simwafunanso anthu omwewo
Little did the so called Atcheya knew that the `kutha ngati makatani’ words will define his own party. History will repeat itself, ask AFORD! Family parties! Enawonso adzathanso choncho, only time will tell.