Email a copy of 'Parliament staff goes on strike: Malawi MPs meeting for mid-year budget review' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Parliament staff goes on strike: Malawi MPs meeting for mid-year budget review' to a friend
Former Malawi First Lady Patricia Shanil Dzimbiri has appealed to authorities tasked to distribute relief items to flood victims to...
Zopusa basi, achotseni, ntchito mulembe ena .kwachuluka mahule kumeneko.
Zopusa! Idislike stupid DDP. Inu poyipatsa mpando DDP yanu m’maganiza zizasintha? Fisi ndi fisi basi angamile m’madzi sadzasintha kukhala ng’ona.
Za ziii
Akupanga strike panopa popeza mwalowa ndalama za donation for floods akufuna adye ndiwo osati anthu akuzutikawo. Yet mukugona pouma, tea daily wamkaka, myama daily pa table, osanganiza za anthu akufa ndi madzi wo…
Tangolembani ena basi,malovatu ife tilipotu ambiri kwabasi.
zopusa basi
Amachita strike anzanu akulira maliro a ma floolds mulibe manyazi osadikira kaye tilire kaye bwanji?
Anthuwa ndi agalu……
Ingowachotsani ntchito basi ” Just fire them all” nothing else.
Zamkutu
apatseni antchitowo maright awo kodi zimakoma kubera mavoti basi uchenjere mpando wakowo upita kwa tupele unangothandizira kubera mavoti ndinena iweyo chilima galu wachabe chabe