Email a copy of 'Pictorial as hundreds mourn Makawa, Malawi hotelier' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Pictorial as hundreds mourn Makawa, Malawi hotelier' to a friend
Malawi National Examination Board (Maneb) in conjunction with Ministry of Education, Science and Technology has finally released the much awaited...
RIP
MHSRIP
May her soul rest in peace. Mawa ndi ife otsala
Rest in peace bola ngati munali ndi Jesus njira yanu ndiyowala.
People must have respect, who can be happy or laughing when you lose your loved one?????????
Rest in peace Alissa, you were always a kind , friendly and gentle soul……. my deepest condolences to Mary & family …. be strong God will guide …
If you have nothing to comment you better keep quiet than posting nonsense. Mhsrip
Mzimu wao uuse ndi mtendera
Iwe nachi zoona ungafanizere anthu a Ku South Africa ndi Ku Malawi? Anthu a South Africa ndi anthu kapena nyama ndi anthu woti munthu WA nzeru zake angawasirire ukugosonyeza kuti. Ndiwe std 7 Drop out. Jewish ndi anthu wolemera kwambiri Ku RSA onaona mmene azimai amavalira pa maliro. Iwe ukusirira agalu eni eni anthu. Ndinu anthu amene mumati eee burger Ku Joni pamene anzungu sadya mkomwe. Kuphoda kulibe kanthu chogumika ndi chitenje ndi duku Mpango, tili nacho chinkhalidwe chathu chotengera cha eni chani? Zitengeranso ndi mmene iwe wathyokera , kufa bulu kapena nkhuku/ bakha . Ukafa papakulu ulibe nthawi yophodera.… Read more »
Kulira sachita kuuzidwa. Zimaphweka zikakhala kwa mzako. Losing a lady of that caliber is unbearable for someone to weep.
Ngati mulibe ndemanga ndi bwino kungokhala chete.