Email a copy of 'PP admits elections loss costly: Matola tells Joy Radio party rebuilding' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

36 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chie
chie
9 years ago

Nawe anthu angataye nthawi kumakomenta za pp lero. Musiileni msonda azikomenta.

EPIGLOTIS
EPIGLOTIS
9 years ago

BAMBO MATOLA CHIPANI CHINAGWA CHIFUKWA CHOTENGA NYANSI KUYENDA NAZO PAMODZI. MASIKU ANO ANTHU ACHANGAMUKA. INU MUNGAMAIKE PANTSOGOLO AGATAMBWE NGATI LEMANI; ULADI MUSSA; ZIKHALE NG’OMA TAONANI PANO KULI CHUUU….IDANYAMUKADI ILI KUNJA…..AMAYI NDIYE ANAWAZA SABWERANSO AKUOPA CHAKUDA

The Country Chief
9 years ago

Chipan sichitha,musathe mau ndi ma comment opusawo,itini phe muone

Richard jafali lion
9 years ago

Pp idatha and sizabwelanso ayi

ujeni
ujeni
9 years ago

Remain strong PP, the only party which tried to embrace the whole country. Let political prostitutes leave, 2019 join forces with MCP and help develop the whole country Malawi.

Mwana weniweni wa Malawi

A Matola mukuti bwanji? Kodi PP iripobe ifetu tinakwiriratu chipani chimenechi.kkkkkkk inu anthu a PP musandiseketse inu nkutenga anthu monga BJ Mpinganjira, Uladi Mussa nkumati muwina masankho? Inu mukuoneka ngati nzeru zolamulira dziko munalibe pamodzi ndi mayi athu aja. A Malawi sitinakufuneni and no matter what PP could have not won that election. Mukamfunse m’bale wanu Gwengwe inu a Matola. Gwengwe kumuuza za PP akhoza kukupatsa mbama coz this PP wasted his time and resources. PP won’t rule Malawi again mark my words.

Richard jafali lion
9 years ago

Adanya kutenga nkhalamba mchipani mwaomodi

Weni weni
9 years ago

People thought DPP will never rule until the time they were reminded kuti Amalawi sachedwa kuiwala. Ingotini pheee

ahoy
9 years ago

Pp siiwina but pitara. Eh headless

Imraan Sadick
9 years ago

Munakanika kuwina muli pampando ma resources onse aboma (at your disposa)l ndiye pano mungawine? Chipani cholamura chantundu wanji kukani kuphika ma Plan obera? Ha ha ha ha ha ha ha nzimayi ndi nzimayi basi!

Arthur G.M. Mtambo
9 years ago

WITH DOUBTS FOR PP TO WIN 2019 ELECTIONS, SORRY TO MENTION THIS BUT STILL NO HOPE OK.

Read previous post:
SA’s wanted criminal traced in Malawi

A businessman thought to have run away from South Africa for criminal offences has been traced to be in Malawi...

Close