Email a copy of 'PP calls for Goodall resignation: Malawi Finance Ministers accused of ‘lying’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

77 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Makhalapwiya
9 years ago

DPP woyeeee.Munya muona osusanu. Chipani koma koma chimenechi.shut your mouth osusanu!!Munya muona nonse odana ndi DPP.mulibe chilungamo inuuu

Mkanaumphawi
Mkanaumphawi
9 years ago

Kuzolowera umphawi! Mukuchita kuwoneratu kuti zinthu sizikuyenda bwino, koma osavomereza. Kakaka ati kusapota DPP. Ndani sakudandaula za kukwera mitengo kwa zinthu. Ndani sakuchita mantha ndi umbanda wochita kulowa kumpanda kwa VP(DPP), Kuchipinda kwa Minister/President(UDF), ………ndi zambiri. Komabe kumangodzipusitsa ndi nonsubsatntial support for a clearly failing DPP. Kodi mukudya support? Think. Osakhalangati olodzedwa.

ellias munthali
ellias munthali
9 years ago

i think old age is killing him ,goodall must be rested i mean force him to retire

pompo pompo
pompo pompo
9 years ago

salary increaments have been effected to narrow the gap between cival servants and the other statuary bodies. Do not accuse anyone including Gondwe. Inu a pp simumaonjezera ma civil servants koma cashgate go to hell simudzalowanso mboma. The rise in civil service ranged from 80% down and the president and his vice and ministers are in that category of civil servants. Why are you only accusing innocent people. Its good that the president and his vice have freezed their hike lets see the others do the same osamangopita kwa tolankhani mkumatinamiza kuti inu ndiye zenizeni. MCP simunasinthe inu munthu kukhala… Read more »

Makhalapwiya
9 years ago

Chokani a Msonda imvi zanuzo pita nazoni uko.Ife ationjezeratu salary.Inu munali kuti? Mumangokamba zopusa zanu pa tvm zisilu inu.PP ndichaninso? Chipani chimenecho chinapita ndi mwini wake Joyce Banda kumanda.Mukamumangira munthu nyumba mpakana penti ya PP chifukwa chani. I’m telling you APM has done a recommendable job about salaries. Pangani kafukufuku abale anzanga muzapeza kuti palibe president mmalawi muno amene anaonjezerapo ma salare ama civil servants ngati APM.So PP don’t waste our time. Munali m’boma momwemo koma malo motilipira boo munali bize kuba ndalama m’boma.Iwe Ken Msonda, Joyce Banda wakoyo sitinamusankhetu wamva? Anapeza mpando chifukwa cha imfa ya malemu Bingu.Akanakhala wabwino… Read more »

Donald
9 years ago

Izi ndiye zanyanya,do you want to me that up to now we don’t have well educated guys who can run that position? Come on my people the old pepper doesn’t sound. Stop of cheating us by posting old ones. I started hearing about Gongwe while I was young running such kind of positions, am now 36 still Gongwe. That’s why our country is not changing.

Chikumbutso
9 years ago

That increment has never happened anywhere in human history

BalakaGuy
BalakaGuy
9 years ago

Ife ationjezera ndalamatu a Dpp,inu munali kuti a msonda ndi joyce wanuyo,ife timakuuzanitu koma osamva,samangokhalira pa tvm kumabwebwetuka,amvekere azungu andiuza,what agood for nothing party PP

anduna
anduna
9 years ago

Don,t blame Nsonda he iz going lightway osati zoputsa zanu mukunenazi

Na Wonder
Na Wonder
9 years ago
Reply to  anduna

Imwe a Goodal Gondwe, fumanipo lekani new blood with new thinking abwerepo apo. Anthu akale ngati inu ndamene mukuononga dziko lathu la Malawi with your old old ideas. What you should know is that you are leaving intelligent people jobless, the people who if used Malawi would have been somewhere by now. You want corrupt people and hate straight forward people who can handle issues without corruption. Please resign and let Malawi be peaceful again without you.

Eye Opener
Eye Opener
9 years ago

A Msonda,kodi Goodal akachoka,muyikapo ndani? inu mungakwanitse kukhala finance minister? other things are easier said than done

Read previous post:
Beware of Facebook business deals: Malawi man tricked

A Malawi farmer in the eastern region district of Machinga by a hair's breadth could have lost fifty 50kg bags...

Close