Email a copy of 'PP don’t be ‘crying babies’ – Lucius Banda' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'PP don’t be ‘crying babies’ – Lucius Banda' to a friend
The romance between Airtel Malawi and the country’s education sector is getting sweeter, better and bigger. On Wednesday, Airtel took the romance...
Lucius wayambapo waiwala zake zija
Crying babes ha ha ha ha ha ha ha ha ha!
Pepani a PP ife sitikuthandizani kulilako za Cashgate sitimadya nawo kkkkkkkkkkkkk
Wise saying lucious. They are really crying babes
Just comfort them and it was not they time!
vuto ndi loti a malawi timayankhula za mavuto a anthu tikakhala kuti sitili pa mpando.Banda is right.zimakhala zondiwawa ndikamakumbukira mmene ndalama za cashgate mmene zimamwazilidwa.who cared by then ndi cash gate yanuyo kuti anthu akuvutika.muzipatala munalibe ndalama.motchale yeni-yeniyi mitembo ya anthu kumawola chifukwa choti compressor yapsya.a malawi tisakhale a mzeru lero.zinthu mziko muno zinayipa kale.Bravo to you Lucius for ur comment.thats maturity in politics.ngati kuli kudyerera bwana pangani choncho ndi nthawi yanu.enawa anadyerera kale za cashgate mu nthawi yawonso and tonse timawona.ena anachita mpaka kuzipha chifukwa cha mkwiyo poziwa kuti zawo zawadera cashgate yatha after kuluza. lucius woyeeee….thats southern behavior.anthu… Read more »
Izi ndi zimene amafuna a Mbendera monga momwe ananenera a Mbendera ku Tally Centre.
Wise ones will take the advise from Lucius Banda but fools will ignore it.
Kodi certificate yabodza imene udalinayo ija, kugwilitsabe ntchito? By the way, who is L, Banda? Is he a politician, musician, or garden boy? Lusiyasi, is nothing @ all. In short, pankongo pamako wanva!!!!
Iwenso public taker tinene kut sumamudziwa,Lucius?Nawenso nzeru nzoperewera ndi2
Owerenga khala maso.Kodi mabvutowo ali ku Malawi kokhako?
kodi form 4 unakhonza tsopano???????