Email a copy of 'PP meeting endorses Mia, Fatchi : Malawi ex-ruling party in its 'deepest crisis'' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'PP meeting endorses Mia, Fatchi : Malawi ex-ruling party in its 'deepest crisis'' to a friend
Bullets FC have got a timely boost in their bid to defend the Carlsberg Cup as top striker Chiukepo Msowoya...
Muyadhlanya mwena
APA NDE PIPI!PI! YANYAMUKA WAKUMPHOMPHO ANZONDA ALI WAYU KHOSI KUTALIKA ULENDO WOSABWERERA JEZEBEL BANDA NDI UYO ANGOTI AKUGWIRA NTCHITO KODI NTCHITO ZAKE ZITI OSANGOTI MUKUTHAWA DZINGWE MUNASUSA KWAMBIRI MMAYI OTEMBEREREDWA IYE MULUNGU AKULANGE
That’s the kicks of the dying horse
A ceaser Fachi ndale anapangira kuti mungofuna kuwabera ndalama basi
Tikati makatani okutha sasokelera nkhani sake ndizimenezi.A PP muwafunse Atcheya akulongosolerani.
Paja a kumpoto ndi amene amayambisa zithutu mu Malawi (i) MCP anayambisa ndi Orton Chirwa(ii) Multiparty democracy anawongolera ndi malemu Chakufwa Chihana(iii) DPP imene a Vipya mosogozedwa ndi a China Wyson Mkochi,Harry Mkandawire anamupasa mphanvu malemu Bingu panthawi yomwe ngakhale azibale ake achi Lomwewa amamuvinila Tcheya Bakili Muluzi amayesa akhalanso ndi mphamvu zamuyaya ngati malemu Kamuzu Banda.
Akamati chipani chikutha pamakhala zinthu ngati zimenezi kulimbirana maudindo
It seems foolishness has no limits what nonsense is this? PP is finished this party is a joke nothing more but a heaven of fugitives.
Agalu inu don’t faulted @ Ngwira Mzomera 4 the north endorsement of Khumbo, why ku mwera they are trying to endorse Mia! Vuto lanu ncani while itazalamule ndi convention not u to judge PP yanyamuka basi, chomupweteka call me @ 992695444 ndikupelekezani ku nyanja ku kakolopa madzi nkukasambisa chipani chako u support!
I hear Peter Mutharika has joined Pp too