Email a copy of 'PP to appoint new secretary general,  Mauludi ‘constructively resigned’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ida pota
ida pota
9 years ago

PP ndiye chani shame on you PP officials.

kabaka mutesa
9 years ago

Osathawa makape inu mumangidwe ndi cashgate mudapanga ija

Gongoni
Gongoni
9 years ago

EISH !!! NDIYE DZI NSARU ZA ORANGE ZIJA, MA T SHIRT A ORANGE NDI ZISOTI ZAMBIRIMBIRI ZA ORANGE ATANI NAZO A MAULIDIWA?

Nankungwi
Nankungwi
9 years ago

Good bye PPeeeeee!!!

Mdicai Longwe
Mdicai Longwe
9 years ago

Inu a Shaibu dziwani kuti audit cashgate report inalembedwa ndi azungu ochoka kunja. Ndiye mukati akumangidwa ndi akumwera okhaokha ndiye kuti chani? Osamangodana ndi atumbuka pa za zii! Ngati mtumbuka ali mbava naye amangidwe basi osamusiya. Ndiye dikirani madzi apite ndipo muziti mwadala.

Tonse ndife a Malawi. Koma chilungamo chioneke basi. Mbava zonse zimangidwe basi. Osayang’ana nkhope kapena kochokera komanso zipani. Tiye nazoni.

shaibu
9 years ago

Mukuonatu amene akumangidwa apa ndi okhaokha akummwera ndi pakati koma achina Kachale ali duuu osawamanga ndipamene timakuuzilani agalu aku mmwera ndi pakati mukamathandizira atumbuka. Iwe Joyce ndiwe amene unagulitsa Malawi ku Mpoto waonatu akumpoto alimonso a cashgate koma akumangidwa ndi abale ako okhaokha akumpoto akowo amene udawaika pamwambawo ali kunja kwa gatecash ngakhale adachita nawo. Chenjezo kwa Chakwera, zomwe ukufuna kupangazo zotigulitsila Malawi kwa PP yomwe ili tumbukalised uwona mopmwe a Malawi amakhaulitsila munthu wotere pa zisankho. Udafulumila kutuluka ku mpando wonona wa zakumwamba kukalowa za usatanazi, you will regret in 2019 chifukwa sitidzakuvotera udzaonanso wekha kuti unataya chipangano. Mmalawi… Read more »

Brainfast Mpoto
9 years ago

it is what it is,mr msonda,tell people exactly that party is now promising to die forever by the way anyone who knows can have a chance to be welcomed by any known party could do so okay?what are the source of the party? if BINGU’S death then shame on you.

Imraan Sadick
9 years ago

Chipani choti sichinawineko chisankho chatha kale ngati Makatani kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk!!

Alfred Munduwabo
Alfred Munduwabo
9 years ago

Maulidi has many cases to answer involving the selling of illegal plots . The guy is a thief and he failed to run his law firm , no need of trusting this stupid idiot.

sauzande
sauzande
9 years ago

Lero mukunyoza mauliidi ku funa john bande as SG.

Read previous post:
K2.1 billion on Mphwiyo’s charge sheet: Malawi cashgate

Former budget director Paul Mphwiyo has been formally charged with two counts of theft and money laundering of K2.1 billion. Mphwiyo...

Close