Email a copy of 'PP's Msonda describes Maulidi as confused, desperate man' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
vincent kaliati
vincent kaliati
9 years ago

DPP ikundimvetsa kukoma ine

Bushi ku Kamuzu Palace
Bushi ku Kamuzu Palace
9 years ago

inu a sibweni wasowa zokamba mwangodana naye musondayo. musonda ndi mneneri wa chipani chathu cha pp amanena zimene chipani chamutuma.
Ife a pp amene timakhla naye kucheza naye kudya naye tsiku ndi tsiku tikumuziwa musonda makhalidwe ake tifunseni tikuuzani. amacheza ndi aliyense wamkulu mwana abambo amai wolemera wosauka angakhale amasikini amamukonda. musonda ndi atsogo athu timamunyadila kambani zina za chigololo mwanama. more fire musonda maulidi sayamika wadya zambiri za amai pano wayamba misala kuluma chala chimene chikumudyetsa satana jabulosi

Sibweni.
Sibweni.
9 years ago

Its Msonda who is disgruntled,desperate,confused & frustrated.Munthu wa nzeru sangamasokoneze banja la mzimai wa mvano ku Chilomoni.mamuna kupanga busines ku Mangochi sindiye kuti mkaziyo ndi wanu.Asiyeni aMaulidi akupanga zandale inu siyani chigololo basi.

MR VIRIWENKO (ZIRIKONKO)
MR VIRIWENKO (ZIRIKONKO)
9 years ago

CHIPASUPASU CHA ANGONI PAMATENGO/ELIKO WAZUNGULILIDWA/BABULO AKUGWA.

MR VIRIWENKO
MR VIRIWENKO
9 years ago

ANSONDA MUWASIYE A MAULIDIO TIWAGWESE.KUNO KULI PHISO WA DPP. IWOWATU ANAGWAPO KALE KUNO KU BT NORTH NDIPO SANATUKULEKO AI.MUKUWACHOSA KUTI MUSALE A YES BWANA OKHAOKHA BASI.AGALU AMISECHE INU.

Wiseman kadakungwa
Wiseman kadakungwa
9 years ago

Musiyeni mzanu, awina basi. Ife tivotera ameneyu kwathu kuno ndiye musamuletse.

katundu madzi
katundu madzi
9 years ago

musiyeni Maulidi Pauloyo ayime awone yekha.kuti tsopano kwake kunatha. bambo Maulidi mudzakomoka ndizotsatila ingosiyani, nthawi yanu inapita ano ndi masiku a anyamaya.

clement
clement
9 years ago

Kodi uyu waufa m’mutuyi amadya koma??? Musiyeni Maulidi azionere yekha paja DPP imawawitsatu ndipo Joyce akudziwa bwino nchifukwa chake anaiwala mwado yake ku Sanjika.

Chikutumbwe
Chikutumbwe
9 years ago

JB analumidwa ndi chakuda ndiye sakufuna atamvanso liwu loti election

Read previous post:
Brazilian Vale’s railway project faces resistance in Malawi 

The future of the railway project under the Brazilian firm, Vale Logistics Limited faces uncertainties as some Malawians in other...

Close