Email a copy of 'Protests over ‘death of healthcare system’ held in Rumphi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Protests over ‘death of healthcare system’ held in Rumphi' to a friend
Veteran journalist and social commentator Mzati Mkolokosa has challenged students pursuing degrees in various arts disciplines at Mzuzu University (Mzuni)...
Amalawi tili ndi vuto loyiwala msanga. kumbukani kuti ndalama zinabedwa za nkhaninkhani m’boma nthawi ya JB, ndalama zomwe zikanathandiza dziko lathu lino. Pano boma likuvutika kuti lipeze ndalama zoyendetsera ntchito zake. zonsezi mwaiwala kale? kusowa chithandizo cha boma ndi nkhani ya tonse ngati amalawi.sinthawi yolozana dzala.
I’m not in support of you.This is country wide agaist Peter. There is no smoke without fire.
MA FELLOW NORTHERNERS WE SHOULD NOT BLAME GOVT.TAKE EXAMPLE OF RALPH KASAMBARA WHAT DID HE DO DURING JBS ERA HE STOLE MONEY THROUGH CASGATE HOW MANY NORTHERNERS WERE INVOLVED IN THAT MASS LOOTING OF GOVT COFFERS.JUST VOTE 4 ME I WILL KILL ALL THE NORHERNERS AND BURN THEIR BELONGINGS IN THE COUNTRY.
Why is it that many CSOs and their leaders are Northerners? To say the fact these gurus have an in-built element of evil minds agaist others gvt. To hell with ur protests. You think we in LL will emulate that. Mwagwa nayo basi,
Kuba too much,,,, ine ndili ku Rumphi komkuno koma Sinddayende nawo chifukwa Kuba ndalama Zaboma ndi mabungwe kwakula, komanso kuwonjezera pamene mabungwe ambiri sakuziwa chochita, monga Ophunzitsa achinyata zinthu zosiyanisiyana M’malomwake ogwira ntchito angozilemeletsa Okha- zotsatira zake chomwe achinyamat akuziwa ndikumwa mowa ndikumakavina ku ma Birthiday paty omwe amakhla akuchitika week end iliyose m’malo osachepera 10 patsiku… Chonchi malawi ndikukhala ndimaganizo ofuna kutukuka,,,, ndizomvetsa chisoni kuti Chilichonse anthu akungoti Pulezideti ndimvula yomwe,,, Tiyeni tizikumbukira kuti azipembezo zosiya-siyana timkapemphera kuti Mulungu atipatse Nsogoleli ndiye tiyeni tikawerenge Baibulo ku mayeyu 7:7 kumatsika,, Tiyeni tikhale ndi mtima wa umunthu. Komanso tikonde Dziko lathu…….
These are the days of survival of the fittest. Days of free lunches are over. There are plenty of drugs in private hospitals.
Aganizireni anthu osauka. Empathize with them. Muganizire muli inu. These people cannot afford to pay bills at Mwayiwathu, Seventh Day Adventist or even kupita ku South Africa kapena ku India mumapita inu kuja mukadwala. Misonkho yathu ija mumadula pa salary ndi zinthu zogula ndi ku Road Traffic, ku Immigration ndi zina zimapita kuti. Someday you will pay for the suffering you are causing
MBANGE NDA NJUNGA NDA NGOMA ZILA JB WAKAMUGABIALANI NYENGO YA KAMPENI. FUMBANI KAMLEPO WAMUVWIRANI IMWE BINA RUMPHI
Sono kuvina uku si mwakhuta kale apa…vindere nadi ivi….
Bwanji osayamba kaye mwasonkhesa ufa ndikukapeleka ku chipatala kenako nkukayenda kunseu kusonyeza kuti inu nanu mbali yanu mwachita, isale ya boma??? Tikaonesesa mwinanso nonsenu apa ndi msonkho omwe simudula kupatula VAT nde muli pa fore front…Its time to be logical..tiyeni tidzuke
typical quota reasoning by Khima @24.. You want these people to dig into their pockets to cover peter’s wastage and theft of our own taxes. these people are protesting against theft by DPP and you know that