Email a copy of 'Queens hospital suspends surgical operations: Malawi water crisis' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Queens hospital suspends surgical operations: Malawi water crisis' to a friend
Mr. 265, one of Malawi’s representatives at this year’s edition of the reality TV show, Big Brother Africa-Hotshots, arrived back...
nkhani ya madotolo achinyengo ija inatha????? zikumvekaso kuti Chipatala china cha CHAM ku lowershire kuli kamberembere. akuti ntchito satha, ndiwaku Burundi,Rwanda,DRC amangosinthasintha akafunsidwa kwao. operation yake thawi zonse ndi ngozi ndipo a Malawi ambiri abvulala mpakan kufa kumene. Akuti a mapanga zachinyengo ndi officals a medical council of MAlawi mchifukwa chake a CHAM anamuposital kutali.
Dzina lake ndi Dr Augstine Ntabanga chipatala chake ndi St Montfort ku chikwawa. Amalawi ofufuza chonde mfufuzeni munthuyu pano akuti akufuna kuthawa poti nkhaniyi yabuka!
Ife takhala tikunena kuti nkhani ya Thawe tathana nayo. Mavuto amenewa bwenzi kulibe chipanda Thawe amene wakhala akuononga ndalama za Blantyre Water Board. Koma boma likumusekelera ma investigation mmene anyambira muja atha liti. It is crystal clear that this guy was stealing from BWB. We are hearing that the sympasizers or Thawe loyalists are the ones who are closing the valves in the water supply system to create an impression that Thawe was performing. Can government please deal with Thawe’s issue once and for all. We are tired of this bullshit. How good is he that you are still hanging… Read more »
bwb do your job faster as you can.
Kumavutika madzi eni eniwa oti mu Shire river alimo ambili omwe akuthera ku Indian ocean
Just refer the surgical patients to other hospitals like ZA central, Thyolo Hosp, Malamulo Hosp and other hospitals. Let not surgical patients suffer because of water.
Let’s get Lilongwe Water Board management to run Blantyre Water Board. Or approach the General Manager who used to appear on MBC TV from Lilongwe Water Board to run the institution I hear his contract expired.
BWB chairman ndi Kapito? Bwanji sakuona mabvutowa? Buns wadyalo limutsamwa pompano. Mademo ake aja am’bwerera tsopano. Blantyre lets march tionetse kukwiya kwathu.
Kaya a Kapito akuti bwanji panopa poti chi banzi chili mu kamwa akulephera kuchitafuna chifukwa chachulukisa.Tiwona Mulungu alupo atimenyera nkhondo even mutatenga onse ma NGO’s koma Mulungu apanga njira paja amatha kusandusa miyala ndiye apa asandusa some of us kukhala a china Kapita ndi Voice Mhone enatu
to some this might sound simple but think of the toilets, the labour ward, operating theatres to have no running water, its a nightmare. no wonder a yesterday a severely pressed patient resorted to pooh in a corrido and a white man had to remove the stuff because we are too smart to clean up our own mess. we can blame the BWB but this is a problem created long time ago, or I should say it is the way the government is run, no priorities, always reacting to things instead of being proactive. shameful! nyanja ya fresh water ili… Read more »
Who is chairing the Blantyre water board now? apa ndiye poyambira ntchito sopano.
Pathetic Malawi. We boast of plenty of fresh waters, actually, we have plenty waters from Nsanje to Chitipa. How can we be having situations like these as if we live in a desert? PATHETIC!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!.