Email a copy of 'Revatalised Bankers move up to second in Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Revatalised Bankers move up to second in Malawi TNM Super League' to a friend
Eleven people, including children, are missing in Nsanje after a boat they were sailing in hit the river bank at...
Pamenepaja Bankerz nkudzandimvetsa kukomaaa!!!!
Team yotsapota ndiye yimeneyi.
Timu yangongolebasi,BB
Imeneyo Nde Saizi Yako Osati Flames
I love you the sky blues. You are a team to trust and support.Pull up the battle is still on.Bravo young chimodzi.
Faka mabankers, reclaim the title
zikuyenderani2. koma anzathu ena nde akulira2 heve. ife mukhala mukutithamangira patsogolopo, 9metres ahead pa mpikisano wothamanga simtunda wochepa ayi. bola tisapunthwe nkugwa osadzuka msanga ndiye mutha kutipeza. tidakamwa wamkaka. mawanso timwa wina mu knockout…
This is the Young Chimodzi I know. FAM munathamanga magazi kumuchotsa ku National Team. Muone zomwe zichitike pano.
Maule womwewo kuti wawawawawaaaa
BANKERS BANKERS BANKERS…..!