Email a copy of 'Robbers hijack OPC vehicle, shoot one' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

28 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
jack mabaso
jack mabaso
9 years ago

what do you expect from this nkhalamba yoyanikidwa pa chingwe?????????????

kabaka mutesa
9 years ago

Zimapheka akamayendetsa ena

Big Kahuna
Big Kahuna
9 years ago

Vytu lolamulilidwa ndi nkhalamba ndi choncho,munthu wa dementia angakuthandizeni??He has no idea.

COLBY MAJON
COLBY MAJON
9 years ago

Galimoto yaku OPC kupangangidwa Hijack kkkk ndie pali malamulo pamenepa kukanakhala kuti boma lathu liri ndimphamvu sibwezi muthu akutchinga galimoto ya atsogoleri athu kaya tiziona amalawi.

nkhedu
9 years ago

sata no more ndithu

Gona n'kuphe sali patali
Gona n'kuphe sali patali
9 years ago

Kodi mesa munkati DPP chitetezo? Boma lamayi citetezo kilibe mmm ai pano nde ndi worse

Wazanako Kowawa
Wazanako Kowawa
9 years ago

Basi tele eniake mukuti dzilibwino…Mapeto ake adzajacka officeyo ndi anthu omwe.musamakonde kuphethira….

Yobe boo
Yobe boo
9 years ago

DPP and Mlahklo team kuba !!!! Mutinyatsa nalo khalidwe lanuli.

Mr.Bambo
Mr.Bambo
9 years ago

Chilungamo!!Chitukuko!!Chitetezo!! Kaya china chija ndi chiyani?DPP woyeeeeeeee!!

Yankees
Yankees
9 years ago

Paja Boma ili chitetezo mchokhwima mpaka galimoto zikubedwabe? Ndiye Bola Mastenitu.

Read previous post:
Mcheka-Chileje challenges Nkhoma’s lawsuit: ‘Marriage issues to be sorted out’

Deputy Speaker of Parliament Esther Mcheka Chilenje has challenge defamation lawsuit filed by her former husband Chief commissioner of Malawi...

Close