Email a copy of 'Robert Chiwamba set to launch new poetry album' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Robert Chiwamba set to launch new poetry album' to a friend
A businessman, a primary school teacher and an old man are currently in police custody in Lilongwe for allegedly defiling...
Tiyeni tinene ZOONA Abale….kodi to RECITE ndi kutani?
Tonse tikudziwa kuti chilungamo chimawawa koma Dokotala Mtabeni walankhula zoona,it was the same with our musicians (especially gospel musicians) they used to play their CDS in the name of live performance. Malawians quickly realised this raw deal and start asking for live performance. Now things have changed for better.
U r vry great! keep de brain folding!
Adokotala Mutuwanusugwila And Zoti Ndiwe M’malawi Ndakayika Mbuzi Yamunthu Moti Pamenepo Ndipolakwika
Chiwamba Kip It Up.Awoatayeni Adzafa Ifayowawa
Malawians let us appreciate others when they do well mmmmh kunyodola basi zaziiiiiiiiiiii……Chiwamba, my favourite
Chiwamba ndi makina a mphepo, amakwanira.
Hear this Mapwiya.Mlakatuli means someone who recite poems from the heart, when one is reading from a copy like what your Robert Chiwamba is doing they cease to be called Mlakatuli.Kupita ndi kupita Ku launch basi kumakaonera munthu akuwerenga mkope?Anyway paja aMalawi we always settle for less.
a dokotala mtabeni, chabwino, inuyo yambani kupanga ‘recite’ ma poem anu from your head tione ngati mungafike pa Chiwamba… Tione ngati athu angabwele ku launch yanu..inxaaa…. Go Chiwamba go!! machine iweyo!! you representing.. ife tili komko to support you chibey!
Umatha composition koma the way you recite zazii. Too much kachibwanabwana mwina poti umayelekeza udakali Ku college. Ine favourite wanga ndi uja amati kunkhondo tea amamwera mjombo kutakasira nfuti. The way he recites ndi chichewa he uses, very talentful. Okoma àtani kuchulukitsa zolira.
Great man of the moment. Keep the fire ???? burning