Email a copy of 'Savala weeps in court after her freedom is curtailed: Calls Malawi cashgate prosecutor Kamudoni ‘bad man’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

122 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mduduzi nyanda
mduduzi nyanda
8 years ago

its a pity such a pretty lady was involved in this stinking shit. had it been that we were able to turn back the hands of time, surely she would choose a different path altogether!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

tanaka
tanaka
8 years ago

Yakula apa ndi msanje….osalephera mumati, ndikadakhala ine ndikana…..!Zinangovuta kuti zinawululika. Inuyo zichedwani ndikuseka anzanu…Khwangwala wamamntha anafa ndi ukalamba…mufa wosadzayilawa million mmanja mwanu..olo mumunene Savala, kaya Lutepo , kaya kalonga, mukuchita msanje apa! Ndani sanabepo chiyambile??? Afisis amantha mukhala osawuka choncho!

Kwateni bolosa
Kwateni bolosa
8 years ago

Kutheka adakweredwanso ulere.

Wapa Teens.
Wapa Teens.
8 years ago

Ndi chifukwa chake atsikana aku 18 anavuta ndi magalimoto.Ambiri nkhani zinali zimenezi eti ?Kumangotinamidza kuti akuthamanga pa town.Mulira kuti mfee mfee simunati.Kamudoni mwayetsa ndi Kasambara.Sakuyang’ana nkhope kuti ndizophoda.The police is going to arrest all of you.

Furious tax payer
Furious tax payer
8 years ago

Don’t blame Kamudoni.He is just following the law.Even the bible you claim to be conservant with,do not allow people to be stealing.Stop cursing Kamudoni kids for their Dad’s profession.That’s how he gets paid to feed his family than having fake companies conning tax payers of million.Don’t be a cry baby to have sympathy towards you.

DZOMBE
DZOMBE
8 years ago

Shaaaaa! anthu oipa kwambiri,inu zoona kunamiza mayi okongola ngati ameneyo chifukwa cha 5%?

Biswel
Biswel
8 years ago

Azimayi a saloon kufera za eni uku nanga 10% mkugawanaso ndi mzako mmmm ndamva chisoni mkazi wokogola ngati iwe ukakhale mundende ndikowawatu ndakhalamo ine ndipo sindifunakoso,bolani iwe unadyako koma ine yongondinamizila aremand yokha yinandikwana sory mama basi limbani mtima there lyf ahead of u

mbuzi mee
mbuzi mee
8 years ago

a dpp nawonso muziafufuza ndi akubanso kwambiri

Thubwelunwe
Thubwelunwe
8 years ago

Kodi ma Prison Warden alembanso liti? Chonde ndilembeni ndizikagadila dona imeneyi. Mwina mkumakadyako nthawi zina

Picker Manondle Cashgate

God loving? Does she really know the commandments of God in Exodus 20? You are mentioning God’s name in vain. You stole people’s money.

Read previous post:
Corruption worsening in Malawi – Survey funded by Irish Aid

A survey report funded by Irish Aid and presented to the Malawi media at Ryalls Hotel in Blantyre reveals that...

Close