Email a copy of 'Sex worker thrown out of a moving car like rubbish' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Sex worker thrown out of a moving car like rubbish' to a friend
In order to achieve self-sufficiency, Malawi government has commenced large scale irrigation farming through Green Belt Initiative to utilize water...
Zisilu
Mahule onse atengelepo phuzilo
Mukunenazi ndi zaku dziko koma chiweruzo chenicheni pansi pano ndikumwamba komwe both need deliverance chiwanda chachigololo chiwamaliza ngati satandizika motero.Megistrate or Lawyer palibe ntchito yawo angolipilisana makhobi pomwe imfayo iziwasatabe bola apapa ali ndi moyo.Issah ndi iwe namwali Mulungu amakukondani munachitazi ndi imfa tembunukani mudziweni Mulungu akukuyitanani chondechonde zaku court izo zakudziko.Mkazi upambana mulanduwu koma pamaso pa Mulungu ndiwe wochimwa chimodzimodzi muzibamboyo lapani satana asakupusiseni ndithu.
munyanya pezani chochita china
Aliyense ali ndi galimoto ayese akweremo olo isakuyenda mbali inayi kukhale munthu ayese kutsegula khomo ya passenger atagwira chongolero and ayese kumu khankha ngati zotheka, uona kuti ayi its not possible ndithu, nde bwanji ikuyenda, one sided story by nyasa, komanso opanda condomu kungomvera zonena mkazi basi
Mwanawanga ku Namitambo mukuticititsa manyazi. Umphawi wotani mpaka kukacita zimenezizi. Mukuyika moyo paciswe. Matenda amabwera ndalama itatha. Choonde pezani Njira zona.
Zakif be like a man,these a normal human being canot sleep with a prostitute wihout a condom.I believe this man knows his status thus thes the law should take its course
CHREA CAN YOU TAKE UP THIS CASE AND DEFEND THE SEX WORKER AS YOU ARE DOING WITH SUCH CASES !!! THIS IS ATTEMPTED MURDER, THIS WAS INTENTIONAL AND HE SLEPT WITH HER PLAIN. IF HE HAS STIs HE HAS A CASE TO ANSWER ON SPREADING DISEASES DELIBERATELY. CHE ISSA YOU NEED TO BE HANGED PUBLICLY.
Zokuti anachita plain akuti ndi mkazi, 10 pin akutinso ndi mkazi, try driving a car n push someone out, open door and kumukankha munthu while driving is it possible izi zama film, mkazi thupi yaikulu mwamunayo ka thupi ka small, not really adding up penapache!!!!
Amwene issa what was the problem, kapena dona siinali boo,,,tell us pliz