Mwachita bwino mwabwera bwana Seydou Keita mudzatithidzimulire ana a flames wa samatha mpira ndi makape heavy, chonde zigoli zisazachepere zisanu please chonde a KEITA!
lewis
9 years ago
mmalo mwa morrocco tipanga host ife maground tili nawo kamuzu bat kalulu civo ndi silver stadium bola timenye nawo afconi basi
Bwana Baggio pilizi makani bwana Keita, asatichitse manyazi
Mwachita bwino mwabwera bwana Seydou Keita mudzatithidzimulire ana a flames wa samatha mpira ndi makape heavy, chonde zigoli zisazachepere zisanu please chonde a KEITA!
mmalo mwa morrocco tipanga host ife maground tili nawo kamuzu bat kalulu civo ndi silver stadium bola timenye nawo afconi basi
Barcelona? AS Roma Captain? CV yovutatu imeneyi. Atipwetekadi. Remember that long range goal in Angola
Acatipwetekanso ameneyu
Amalawi Tisaope,keita Ndidzina chabe nayenso ndi munthu ngatiinu nomwe,ofunika kungolimba ntima,ndizotheka kugonjetsa Mali.
NO FEAR, GO MALAWI GO! YOU CAN DO IT!
Kodi nkhani ingokhala ya kondowe ndi kanyenda mmene mwayambila kunena ngati ma player enieni ma journalist akumalawi kusowa nkhani SHUPITI
ok