Email a copy of 'Shanil warns against abuse of relief items' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

11 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Andy Phiri
Andy Phiri
9 years ago

Mayi wathu wafuko waku BK komanso MP osadzitukumula timakunyadilani nthawi zonse. inu Mulungu anangokudalitsani kuti mudzichita zachifundo ndipo musasiye kuthandiza ngati mmene mumachitira kale. Mphatso simachepa ndipo mwathandiza anthu ena dela lanu omwe akhudzidwa ndi vuto lama floods. Ndimawelenga news paper ya Mkwaso ndawonanso nkhani yoti munathandiza ku Cecelia Youth Centre ma buku kuti ana adzilimbikira sukulu. kumeneku ndiye timati kutumikila anthu omwe anakusankhani osati kudzikundikila. Aphungu ena boma la Balaka sakuchita ngati mmene mukuchitila inumo. a first Lady Mayi Mutharika atengere chitsanzo cha inu osati kudzathandiza anthu ku Bk ndi soya piceases mmalo mowapatsa ma bucket ngati omwe munapelekawo.Bravo… Read more »

Jescano
9 years ago

Mayi wathu musasiye kusamalira anthu pokumbukira kuti pali mawa mkubwera bwino.

Mc Nyopex Tuzuke
Mc Nyopex Tuzuke
9 years ago

timaganizo tanzeru ndithu koma tima bucket 50 basi ayi kamphatso sikachepa koma mukanakapempha kwa Bigman Chair akanakuthandizanitu amane aja ndi kuchitekete, kumachenjera patown mai

Fathi Alshehaab
9 years ago

zilibwino mwayamba bwino

Mai ndi Mai
Mai ndi Mai
9 years ago

My favourite first lady. Usually in chitenje outfits with duku on. No fanta face and coke hands. No phyuu lips (more than mzungu). Just plain Nadzimbiri. Kubvala chonchi osasiya. Kusunga khungu lako osasiya.

WINB
WINB
9 years ago

nanu ingothandizani musachulutse phokoso…..

asambuka ndekuti chani???
inuyo ngosasambuka??

Mtonga wa Mtonga
Mtonga wa Mtonga
9 years ago

Former First Lady…Koma yaaaaaaaaaaaaaaaaaa!!!!!!!!!!!

Kalonga Gawa Undi
Kalonga Gawa Undi
9 years ago

thumb up former first lady

shame
9 years ago

ndie mwati ma plasma akuonekawo mwawapatsaso anthu………ai ntchito zabwino izi zachifundo enaso atengelepo chitsanzo..

zingayambe kuyiwalika
zingayambe kuyiwalika
9 years ago

Kodi chemwali ake a izeki , mulipo ? Ndakunyadilani !!!!

Read previous post:
‘Help,’ pleads family of missing Malawi woman Taona Kankondo

Taona Kankondo 29, daughter of a well known Malawian author and lecturer, Dede Kankondo, has been missing since last month,...

Close