Email a copy of 'Shoot to kill: Malawi Police shoot dead two habitual criminals' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Shoot to kill: Malawi Police shoot dead two habitual criminals' to a friend
Minister of Youth and Sports Development Grace Chiumia has said government would not name the state-of-the-art stadium currently under construction...
Aphedwe basi
Akuba ndi mfuti kapena kuti ndi zida zoophsya aziphedwa basi
KILL THEM THEY ARE ANIMALS
you may be happy for what has just happen but what if it was your brother or your son
verygood well done zimene tikufuna ife
ndiye zimenezo
Akaphedwa A Police Ndie Mumasangalala Koma Awa Akuba Oopsa Ndie Mukuti Police Ndiyoyipa. Zigawenga Zikadza Kunyumba Kwanu, Mumasekelera Inuyo?
Mukufuna kumaweta zigawenga bwanji? A Malawi tiyeni tikonze Malawi wathu kukhala wa mtendere. Phani onse achifwamba mu 2019 tisadzalowe nawo ife a MCP.
What about the names of the thief’s?
Killing is asin dont forget bible says , why dont you arrest them. God will punish you who shoot them.
Kuba ndi nfuti aphedwe basi!agalu amenewa