Dru Hill? Lero? Koma abale mukuwatengela ndani zimenezo? Ndiye mbola yake a r&b mukawaphatikiza ndi skeffa chimoto heeiish koma a organiser akewo? Mudakawaphatikiza ndi mafana ngati Theo Thomson or Sonye. Sisqo lero? Eei mundikumbutsa ujibidi utangoyambika kumene pa Malawi, ndili form 3 pa chipoka sec school mu 2001. Momwe amavinila achina prince simwaka, Bahat Gama.
Skeffa Ndi Dru Hill. Country rat and Town rat
Koma zilipo. Mpaka Skeffa.
Thong song in Malawi? Hehehdeee…..
So this is where the poor country will waste its forex?
lol
Why skeffa chimoto
Akakhala mu form amatiswaya akatha ndiye ‘we r comin’, we r comin ‘ zachamba basi mukalowa nokha zimenezo bola dollayo kukamenyetsa blowjob pa Mbowe!
How can you mix Dru Hill with Skeffa? We’ve Taygrin and alot of urban musicians. Wake up Mr/Mrs organiser.
koma ndiye!
Koma zinthu zaphwekadi izi, kodi gulu limeneli lilipobe???????? who proposed this idea????
this group was famous in the 90s. Kaya tikaziona konko