Email a copy of ''So what' artist Dan Lu announces engagement plans' to a friend
Loading ...
Email a copy of ''So what' artist Dan Lu announces engagement plans' to a friend
Sponsors of the country's top flag league, TNM have rolled out a national campaign aimed at engaging and wooing football...
Al the best broh,dziko linavuta ili likufunika kupeza okusunga,…
Ndinthawi ya malova tsopano. Yobetcha inatha kalekale, Onsewo ali pa #FreeTransfer kuchokera ku mabanja awo. Mahuleeeeeeeeeeeee!!!!!!!!!!!!!!!!
Wishing you all the best, padziko lapansi palibe wabwino ndipo wolankhula azalankhula, Dan Lu panga zomwe mtima wako wasankha anthu womwe sakufunila zabwino akakolope nyanja
Mwamuna amakoma ali kutali ada, ukakwatirana naye ndiye umati bola yemwe uja unamanga naye ukwati uja
Inuyonso muli nayeyo ena anatopa ndikumpwala
kkkkkkkkk
Osamusiyansotu uyu pls
kaya amwene aliyense ndi ochimwa
Ayi zabwino zonse pa timasiku tomwe mukakhale ndi moyo chifukwa apa ndiye aliyense wavala bomba latimke nawo basi. Ikadakhala gemu ya manoma tikadati muli mumapenati basi.
Komatu nde zavuta apa…..everyone iz talking…..comment reserv…
Zilibwinotu apa amwene