Email a copy of 'Speaker sends stern warning to misbehaving MPs: Kaliati, Kabwila clash' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Speaker sends stern warning to misbehaving MPs: Kaliati, Kabwila clash' to a friend
Health minister has said government is worried that the number of women visiting Christiam Health Association of Malawi (CHAM) hospitals...
I love kaliyati for what she is ,strong woman like her wow Malawi is lucky for you Dear.ndipo sulakhula zopanda mzeru ur always speak importance to our county only kukumvetsa ndikomvuta sinanga alibe zeru.
Iwe jesse mmmh izi zimakumvutani ingosiyani ndale mukalime mwina kuchuka ndiulimi koma osati uzilimbana ndi adona ayi ,ukafuse mbuye ako atembo akumudziwa bwino Dona kaliyati.zinali bwino komkuja ku chacco osati ndalezi ai .
AZIMAYI AMENEWO AKU MALAWI, CHONCHO TINGATUKULANE OLO TIKUMANAMIZANA KUTI TIKHALE MMA UDINDO APAMWAMWA 50 – 50 COMPANY ITHEKA APA? WHAT WILL MEN THINK OF US? ADZINGOTI ANALANDANA AMUNA NDIYE PHYIPHYI ZAKE ZIKUTHELA KU PALIAMENT. ONSE NDI MA SALVAGE OKHAOKHA WINA OPHUNZIRA WINA OSAPHUNZIRA ONSE NDI DZINYALALA.
Respect to hon kabwira ur more than caurageous.
Do not argue with a fool because people may not notice the difference! Empty tin arguing with a full tin! JK please do not lower your standards to those of PK, she is so dumb!!!
hmmm folks, penapake. God loves u both. hope u know that.
the brainy and brainless
Breaking News, Hon Patricia Kaliati practices Satanism. 100% true. Check it our!
koma jersey ndi wokwatiwa?
Professionally, educationally, morally Kaliati must not talk when Jessie has talked. Educated people respect the hierarchy but thanks Kaliati is not educated. To understand the hierarchy. Vuto ndi ma constituency anu, mumangotumiza zimbayambaya zosaphunzira basi ku Parliament. Makamaka DPP/UDF kum’mwera uku, many MPs have basic educationunlike other parties. Timawanena a Chewa kuti ngosaphuzira but look at the cream sent to parliament! At least a first degree. Check the level of education for the funny &confused MPs. This mixture has failed Malawi altogether.
mwatikwana ma politicians athu this is not wat we voted you for. nyasi zanuzo ai