Email a copy of 'Staff at National Bus Company demand to meetu Mulli or down tools over salary' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Staff at National Bus Company demand to meetu Mulli or down tools over salary' to a friend
Malawi Police at Balaka are keeping in custody a 31 year old man for allegedly being found with a rifle...
pena vuto si mulli koma mbuli zomwe zinapasidwa maudindozi.you will see zikatha zimenezi achosa ena mwa ogwira ntchitowa.can a holder of Jump Carefully be a branch manager nowadayz….
Stupid minded people with full of immorals think like that, how do u think malawi could develop with such pipo like u ? U r stupid.
Abwana Aganize Bwino Tsopano Asamangotukwa Zonunkha
Abwana Aganize Bwino Tsopano
Bingu atangomwalira, ma bank aku Malawi, especially MSB, anamasulidwa mu msinga za Mulli . Zonse zinkachitika zija siunali ukadaulo wa bizinesi ayi . Zinali ndalama zotenga moopyseza ku ma bank . Other well deserving Malawian business people were being refused loans by the banks coz Mulli amakhala atasesa ndalama zonse . Lero ndi izi .
Koma AMalawi ngati mumalandira pa 10 mwezi uli wonse ndiye kuti pay day anasintha palibe vuto ,ndiye kuti mumalandira pakapita 30 days ngati wina aliyense ,basi mumafuna kulandira pa 20 chakuti basi ngati ulandira pa 14 mwezi uli wonse kaya pa 30 mwezi uli wose Pali vuto bola papite 30 days .
kuganiza mopusa kumeneku. Pay days should be consistent for proper planning.
Atitani if u hv no sense making point jst rman quite than to write RUBBISH…WAMVA KATUMBU IWE
Titani if you hv no point jst kip quite
Mulli ameneyo . Nthawi ya Bingu anali katswiri wa business . Lero wasunduka kape weni weni . Business ya mtundu wanji yodalira kuti ku State House kuli ndani?
If you are paid on 10th every month then it makes no difference to be paid on 25th every month. It is still one month.