Email a copy of ' Standard Bank gives K8m to Nkhoma University in Malawi ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

11 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Livulezi river
Livulezi river
9 years ago

Mr Manyathi!!!! The money is just too little considering that the bank had recently recovered over half a billion kwacha which was stolen by the bandits. and here you are thanking god with a meagre K8m. Is it fair??? Ndi ya mpingotu iyi!!! It should have donated at east K50 million not that amount. Anyway, poti ndizopatsidwa, ndingotibe zikomo ” BANKI” . Poti ndiye kuthokoza kwa ife Angoni!!!! Akanakhala menthe tikanati zikomo ” PHIRI”

naphir
9 years ago

imwe mwatani, musiyeni munthu wa ku Kasungu.He did not ask for it

yohane
yohane
9 years ago

Guys koma ma university aku malawi eeeeeh maphunziro alibwino koma ma building eeeh nzungu kulowamo osamvatu kalikomse kuona ngati chimugwera. Azibusa osabanso ndalamazi musativute ndi ma paper sunday.

Chemjambe
Chemjambe
9 years ago

Kodi mwati ili pati pati university imeneyi? tikungomva ife zakuti a Nkhoma synod anatsegula university

KEY CUSTOMER
KEY CUSTOMER
9 years ago

THE CORPORATE UNDERSTANDING IS TO ASSIST INSTITUTIONS ONLY ON THE CENTRAL REGION, SCHOOL ME IF THEY HAS BEEN OTHER INSTITUTIONS ASSISTED IN SOUTH EASTERN, SOUTHERN AND THE NYIKA REPUBLIC BY THIS POPULAR BANK

Thoko Banda waku Thyolo
Thoko Banda waku Thyolo
9 years ago
Reply to  KEY CUSTOMER

Iwe key customer, mpaka “they has been”? unaphunzira free primary school nthawi ya tcheya eti? kkkkk!

Yobe boo
Yobe boo
9 years ago

Zachilendo koma EEEEEh Mpaka NkHOMA university? maphunziro ndiye apheka. Kukhala zenizeni kumeneku? Ndakayika

Chemjambe
Chemjambe
9 years ago
Reply to  Yobe boo

Adya ndalama zimenezi azi Busa akumeneko ndi anthu adyera heavy!

Mbolo Sidwala
Mbolo Sidwala
9 years ago

Please help. Prof. Kanyama Phiri? Chancellor of Nkhoma University? Is he not the same who is V.C of LUANAR? Sipali conflict of interest apa?

eye eye
eye eye
9 years ago
Reply to  Mbolo Sidwala

ndiomweo ndithu Vice chancellor LUANAR, chancellor Nkhoma University…..eeetu…only in Malawi….Vc..UNIMA is also Chairman MUST in Ndata..eetueeeh…..roundand round we gomanaging this university and then guiidng another university….

Yobe boo
Yobe boo
9 years ago
Reply to  Mbolo Sidwala

AKANYAMA PHIRI, UMBULI UMENEWO, MUKUPANGITSA KUYIKAYIKIRA KWAMBIRI UNIVERSITY IMNEYO. MUKUNDIUZA KUTI ANTHU ENA KULIBE KUTI NOKHANU MUKHALE CHANCLOR, VC, CHAIR KULIKONSE? AAAAAAAAH! MADALA UKAPE UMENEWO, MUZIKANAKO ZINAZI OSANGOPHANGIRA ZONSE NOKHA.

BIG PROBLEM WITH OLD SCHOOL BOYS. NZACHIKALE ZIMENEZO.

Read previous post:
Malawi Electoral Commission receives Misa golden key award

The Malawi Electoral Commission (MEC) has been voted as the most open public service institution and has been give the...

Close