Email a copy of 'Sulumba remains a Nomad, not joining Nyasa Bullets - Rashy' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Sulumba remains a Nomad, not joining Nyasa Bullets - Rashy' to a friend
The country’s consumer and human rights activist, John Kapito has condemned government for being clueless, helpless and inconsiderate in finding...
Mukamukakamira Adzakuvutan Apite Komwe Akufunako Chifukwa Adzayamba Kufuna Zambiri Kut Muzmupembedza Musiyene Amenye Yomwe Amasapota
Sulumba ndi dolo nyelele woye chaka chino ndichathu basi
A NGAUMA WHAT DO MEAN WHEN YOU SAY PPLE TEAM? YOU WANT TO MEAM AMA TEAM ENAWO SI ANTHU ANTHU NDINU OSUTANU
NYERERE FOR LIFE SULUMBA SIKUTI TUMUKAKAMIZA KOMA WAONA YENKHA KUTI PA BB PALIBEPO NKHALIDWE UMALENGE DEAL MUSANA GWIRIZANE PWINDA INU ETIIII
Tatenga cup 2 times without sulumba apite we dont fear u nanga mumati alibe ntchito mukumuliliratu apa wakuwonetsani kuti ndi dolo
sulumba will be psychologically affected
Nyasaland BB, Kodi kupupuluma mudzasiya liti? Player wina aliyense wosewera bwino basi ndi wanu.Pano mumanena kuti mutenga STD Bank cup, tengani. Kuba ma player basi. wooooooo!!!!!!!!!!!!!!!!
si wa noma ndi wa bt utd mukusokoneza inu pliz
chamba chikakupwetekani musamathe nacho ,mau pamenepo ndipamene taziwa kuti nyerere is stuppid team sulumbao ife tikanakamusula osati kutiphunzitsa ai
A bullets kupupuluma too much sulumba cannot advocate for smoking mwagwa nayo neba
Manyi anyerere mukulongola chani .simumati Sulumba alibe ncthito, zitsiru wapita basi ku BB