When you see a white man coming close to you,eeeee open wide your eyes, akubera ukuona. See what is happening with Kayekera mine and all these mines being opened. Wake up Malawians when you sign deals with Whites. They like foolish guys not clever guys.
Guantanamo
8 years ago
Thanks, Surestream, for ur contribution to Mw futbol. Ur 1st born is Wizard foot ball club. Zikomo kwambiri!
moses makoko
8 years ago
Kikkkkkk! nkhani inali yofuna mafuta sha! mzungu ndi mbava!
Kandapako
8 years ago
Zitsiru, agaru inu a fam, osawononganso ground limeneli lisamaleni agaru inu, ntchito ndikuba basi pachi………….panu mukawononganso mbambadi.
Geoffrey Lwanja
8 years ago
They have helped fooyball development.Anthu ena basi munabadwa osokonekela.Simuzathokozapo basi.Mumalephera kuwabela azunguwa kapena.
May somebody contact Major Prophet Bushiri.He is helping youngstars in a similar wau in RSA.Where are they going now.We may lose these youth to drug abuse.An idle mind is the devils workshop
Otanjere
8 years ago
Amalawi amene azabwere osakubelani nde ndani? Nde bolanso awawa akanaba uku akuthandiza. Paladin ku Kayerekera inakubelani koma inathandizapo mpira? Mota nde ndi iyi ingothandiza zokhuza ku Ndata. Osamangobwebweta. Amafuna azizaba ndekuti chani?
Calvin A.C. Banda
8 years ago
There idea was very good. It was the only campny that have supported the country’s development as far as sports is concern. May they continue giving us support even though they are going.
ELLINA MAONJERA
8 years ago
KKK NZUNGU WALEPHERA KUBERA MMYASALAND KKKK WAMANGA PHUKUSI LAKE WAVAYA KU ULAYA KKKK
When you see a white man coming close to you,eeeee open wide your eyes, akubera ukuona. See what is happening with Kayekera mine and all these mines being opened. Wake up Malawians when you sign deals with Whites. They like foolish guys not clever guys.
Thanks, Surestream, for ur contribution to Mw futbol. Ur 1st born is Wizard foot ball club. Zikomo kwambiri!
Kikkkkkk! nkhani inali yofuna mafuta sha! mzungu ndi mbava!
Zitsiru, agaru inu a fam, osawononganso ground limeneli lisamaleni agaru inu, ntchito ndikuba basi pachi………….panu mukawononganso mbambadi.
They have helped fooyball development.Anthu ena basi munabadwa osokonekela.Simuzathokozapo basi.Mumalephera kuwabela azunguwa kapena.
May somebody contact Major Prophet Bushiri.He is helping youngstars in a similar wau in RSA.Where are they going now.We may lose these youth to drug abuse.An idle mind is the devils workshop
Amalawi amene azabwere osakubelani nde ndani? Nde bolanso awawa akanaba uku akuthandiza. Paladin ku Kayerekera inakubelani koma inathandizapo mpira? Mota nde ndi iyi ingothandiza zokhuza ku Ndata. Osamangobwebweta. Amafuna azizaba ndekuti chani?
There idea was very good. It was the only campny that have supported the country’s development as far as sports is concern. May they continue giving us support even though they are going.
KKK NZUNGU WALEPHERA KUBERA MMYASALAND KKKK WAMANGA PHUKUSI LAKE WAVAYA KU ULAYA KKKK
muyamba kugawa chimanga kkkkk
Amafuna azizaba? Achita bwino kuwamana licence. Folk off