Email a copy of 'Synod says Malawi federalism movement ‘unstoppable’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

68 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Atate says
Atate says
9 years ago

Anthu a kumwera ndi pakati mulibe nzeru. Atumbuka mwakhala mukuwadandaula nthawi yaitali kamba ka kudzikonda kwao. Lero akukutsanzikani akufuna adzipita kwao, inu mukuti ayi. Mumadandaula za bodza eti? Let me remind you Quota System came becoz one tumbuka in the University council was replacing names from the south and central pa selection list with northerners. The secretary (was not a tumbuka) reported it to authorities and went up to the president. Today even during MANEB examinations, security is heavily relaxed in the north ( no police etc, The Security officer is Tumbuka) and there is rampant cheating there (anzeru). Ku… Read more »

Aninto
Aninto
9 years ago

Am a northerner who strongly wish for northern secession and not federal system of govt. I humbly urge you servants of God of Livingstonia synod to help northern people gain political independence Amen.

Aninto
Aninto
9 years ago

We really need civic education on the subject of federalism bcoz most people think that the system is division-breeder rather than social-economic equality promoter.

Thunthu mpwiniha
Thunthu mpwiniha
9 years ago

Fedulo si yamtundu ayi koma kukoza machitidwe ndi kaendetsedwe kabwino padziko lathu ife ngati a Malawi.Mbuli zokha ndizimene zingamakane motere ndipo atsogoleri athu a Mpingo pangani zotheka kuphuzitsa nkhani imeneyi monga kalelija pa nkhani yazipani zambiri Mulungu akuthandizeni ndipo tituluka mudziko lakusadziwali

MTHUTHA
MTHUTHA
9 years ago

Livingstonia Synod, asakukudziwani ndani anthu a tsankho ngati inu? zochitika zanu zoti ndiinu opemphera ayi ndithu…ndiinu nomwe munakangana ndi synod inzanu, Nkhoma mpaka kukanika kugwirizana mpaka mwamanga ma church mMalawi monse mpaka ku Mulanje. anthu a dyera, osauzika, osamva, amakani opanda chikondi. pano mwati mulowenso ku dziko. Joyce banda wanu akukutumaniyo mupindula naye chani?

You are a disgrace as a church and you just show that God isnt in your synod. too bad for you honestly

MAMA
9 years ago
Reply to  MTHUTHA

MLOMWE KUDZIKONDA KULIMBA MTIMA NGATI MFITI YAYIKAZI !ANTHU AKULIRA AKULIRA ZOTI ASINTHE NJEEE WAMANGA WAMANGA MULOPHWANA KHANYUWA !! KAYA BAIBULO OR KORAN YAKE YITI YOPANDA NAYO CHIKONDIYO NDI UMODZIYO ???

Havez al Sahalaaw
Havez al Sahalaaw
9 years ago

Koma chonde zitsime za mafuta mutigaileko chonde ndagwwila mwendo wanu.

linga
linga
9 years ago

Zitsime za mafuta? Don’t worry. Northerners are just 3 million. Chuma cha oilo sitingachithe tokha. Alomwe musadandaule. Tizakugailani. Musaiwale kuti Asena alinso ndi zitsime zawo ku Lower Shire. Koma tizaonetsetsa kuti chumacho chikutula ku North chisanafalikire kwinako. Eyaaaaaa!!!!!!!!!!!!!!!. Koma, siyani kuti tukwana

sir mzungu
9 years ago

Mvula zakale, Kodi federalism ndi chida chogawira dziko ngati? zinthu ngati munthu siukuzimvetsa ndi bwino kufunsa.

All those who need civic education on federalism should call the conern body.

Barton Chikaya
Barton Chikaya
9 years ago

Mwana akalirila mnyanga ya nsasi,musemereni ndikumupatsa kut imufotere yekha.

AMalawi tiyeni timve pempho la anzathu awa a Kumpoto, ndipo zigawo zonse zipange referendum. Zomwe zizatuluka mu mavoti a referendum ndi zomwe tonse tidzatsatira.

PAUL MHANGO
PAUL MHANGO
9 years ago

NO Federism,NO Secession,NO room for LIVINGSTONIA SYNOD. I know our Reverends they so political and are confusionist,they are always freedom fighters but get nothing.Adakanganapo ndi Nkhoma synod,Bingu and here they go again.No wonder Livingstonia synod becoming a political party.PREACH SALVATION and see what GOD will do to our Nation.NO FEDULO,NO SECESSION, ONE MALAWI.

MAMA
9 years ago
Reply to  PAUL MHANGO

LET THE PEOPLE OF THE NORTH DECIDE LIKE SCOTLAND WHAT ARE YOU SCARED OF ???

jb
jb
9 years ago

I am for a federal state – it will at least give each region the power to determine its own destiny in terms of social development. Decentralized authority to run social services : agriculture, education, health, road networks, etc will enhance accountability of public officers. We are tired of cashgate and NO DEVELOPMENT.

Read previous post:
Plot to cage JB as Lutepo seals ‘amnesty’ deal: Malawi cashgate doctored report goes viral

The Democratic Progressive Party (DPP) government has taken its brinkmanship game to another level by resorting to cook up evidence...

Close