Pakufunika kumutenga ku National team yathu during Zimbabwe’s game
pilirani maida
8 years ago
keep it on gals….. :
Kapala
8 years ago
Anzatu ku northern Malawi ali boo, ku mpira no1, maphunziro no1. Koma kwinaku eee kubelekana ndiye no1.
MCHEMO
8 years ago
LET’S SUPPORT GIRL CHILD HERE AS MALAWI WANTS – BUT NOT TREADING ON THEM AS THE CASE OF A CERTAIN LECTURER IS FACING FROM HER OWN COMPATRIOTS WHO WANT HER TO END HER PHD STUDIES IN THE LINE. PUSH DOWN FACTOR. SUPPORT GIRLS LIKE CHAWINGA TO EXCEL
Mtawali must consider this player she is a man se can score try to pair her with Sulumba
Adam christon Masamba
8 years ago
Malawi ili patsogolo kwa akazi, omwe amasewera mpila wawo kunja. Kunetball kuli Mwawi Kumwenda, pamene kufootball kuli Tabitha. Pamene kwamunawa aaa, south africa yokhayokhayokhayokha eish, Tabitha kp it up, ur best way.
Pakufunika kumutenga ku National team yathu during Zimbabwe’s game
keep it on gals….. :
Anzatu ku northern Malawi ali boo, ku mpira no1, maphunziro no1. Koma kwinaku eee kubelekana ndiye no1.
LET’S SUPPORT GIRL CHILD HERE AS MALAWI WANTS – BUT NOT TREADING ON THEM AS THE CASE OF A CERTAIN LECTURER IS FACING FROM HER OWN COMPATRIOTS WHO WANT HER TO END HER PHD STUDIES IN THE LINE. PUSH DOWN FACTOR. SUPPORT GIRLS LIKE CHAWINGA TO EXCEL
Atumbuka sianzathu pankhani ya luso labwino ndithu tikungochedwa nawo anthuwa uuuu
Mtumbuka ndi dhilu.. Kafunseni mwayi kumwenda.
Paja ndi Tapita Mulukunuwa eti?

bravo