Email a copy of '‘Take off fear’, Gospel Kazako on CNN: Malawi media mogul' to a friend
Loading ...
Email a copy of '‘Take off fear’, Gospel Kazako on CNN: Malawi media mogul' to a friend
Ivory Coast finally won the African Nations Cup after a decade of close calls as they edged neighbours Ghana 9-8...
Manyimwekha
Kip it up Kazako …U hv don maverous
U hv changd lives of many malawian
May almity bless u abandantly
kodi nkhani yonyengayi yachokera pati zachamba
Start small but always think big,thats the rylic l lik on ure story,we ar proud of you,we need people like you,people who can kip malawi flying,go on and on,.and akazi akumalawi kutengeka,ngati wagwa mbale nawe mpata ulinawo ogwila nawo ntchito,lets support gospel kazako guys,and think where he is from,radio station,now its television,ena ndalama alinazo koma amalephela kupanga entertainment things ngati izi,we love you kazako,,kip ure future and ure business grow up,.
MAMUNAUTI SANYENGA??? ALIPO AMUNA AMBIRI AMENE SANYENGA.
GOOD OF YOU KAZAKO TO-MORROW OTHERS.
Mwamuna uti pa malawi pano amene sanyenga? Adzinyenga azibambo a dzidzukulu nde mukanene Gospel, young and handsome. Kambani zina abale.
a Malawi nsanje timasangalala tikaona wina akuvutika. Pano tikukamba za CNN with Gospel koma mukumufukula personal life yake chifukwa chani? Mwamuna uti sanyenga, ndiuzeni ndipo give me two weeks ndimufufuze. If he is single, thats none of ur business. Akaziwo amamuputa dala chifukwa if he has a string of g/friends, nde kuti akaziwo akufuna. Mkazi mbambande sangataye nthawi ndi mwamuna wa akazi ambiri koma angati amakhala naye nthawi. That means akumufuna. He is a man, dont forget. Amuna pa malawi pano amasiya mkazi mnyumba nkumakanyenga nde munene wopanda mkazi. Takambani zina a Malawi.
I guess more money more problems. Gospel should have remained a poor boy and people would have liked him. Its not his fault women throw themselves at him. He hasn’t raped anyone so what he does with consenting adult women is his business. What would you do if you were in his shoes? It comes with the territory. Try and make your own impact somewhere or if you cant then Just live your life eh eh eh eh eh eh! #ilovemusic
am very proud of you mr kazako, u inspires me alot.