Email a copy of 'Tay Grin says Chipapapa video has cost him K5.5mil' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Tay Grin says Chipapapa video has cost him K5.5mil' to a friend
Many times Christians have faced opposition and have wondered why God allow certain things to happen in their lives. God...
A Malawi umbuli. Shooting a music video costs a lot of money than recording a song. Think of fees for the collaboration, flight tickets accommodation.For example.It cost $200,000 to do a collaboration with NiC Minaj. MK5.5 mukuti yachulukayo is a mare R137,000. Please don’t think like chickens mukutichitsa manyazi ndi nyasi mukulembazi. Any way big up Tay Grin. We are behind you I hope other artist wil follow.
All the best boss
So 5.5 million what? ZA cashgate mukunyadiranso? Mukathandizenso kuba ma vote ena adzapatsani cheke china. Paja ndinu munaitana Ligomeka kukakuthandizani kuba, pano mwapanga hire company ya kunja.
nsanje ai mfanayu wadza ndi lumo lakutwa
MALAWIANS NSANJE BWANJI?TIYENI TIZIYAMIKA PAMENE ANZANTHU AKUOPANGA ZABWINO EISHEEE
ndiye……titani ife …….mabi basi
man do you want to tell me kuti 2FACE amadaliranso nthumba mwanu? anyway mwina mudzatenga nawo award.
Kunena zoona, who shoots Videos for 5 Meta? kuuza ana chani.
Big up T. Grin. Umatichotsa manyazi makamaka ife anthu wofuna za boo !!!!! takunyadila. Ife kuno ku SA we will fully support you.
Mwationjeza man… 5.5 million nkhani yake??
inde ndalamazo ndizanu koma ka video kanuko kangokoma kwa mwezi umozi bas.. bola ikanakhala film bwezi tikuonebe mpakana kale kwambili. Nyimbo yakupangisani phuma kwambili, mwayimva kukoma.