Email a copy of 'TCC says Malawi Kwacha gain setback in tobacco selling' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

31 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ngala mountain
ngala mountain
8 years ago

Bruce Munthali ndi amene amauza aZUNGU kuti azigula alimi pa mtengo wotsika kumanamizira kuti kwacha yakwera mphamvu .Munthu woipa ameneyu adzafa imfa yowawa musiyeni .Nthawi zonse ali minimum price ndi $0.85 .osawasiya a zungu kuti agule fodya pa mtengo umene akufuna ,koma chi Munthalichi kuchita kuwaletsa azungu kuti asadutse $2.10 .Ife tidzangosiya kulima fodyayo tiwone udzasowe omuzunza.Tatopa ndikubweredwa.koma tikati tikagulitse fodya ku Zambia kumene kuli mitengo yabwino mumatilanda fodya tisiyeni tikagulitse fodya wathu pa $8.50 KU zAMBIA KUMENE SABWERA ALIMI STUPID Munthali

Maxwell Nsani
Maxwell Nsani
8 years ago

People, There is no tsamunda dictating our kwacha fluctuations as the others have said. its simple demand and supply. Play your role in making the diversification mantra come to reality, that way the appreciation of the kwacha does not only happen during the tobacco selling season. Encourage more tea, coffee, paprika, and many others after the tobacco market or along side it, so that we do not have a forex drought annually after the tobacco season is over. This is what Bingu used to call `…a basket of products`. Some of the current ministers were there when he used to… Read more »

kadokera
kadokera
8 years ago

Bruce umangodziwa kutumidza abale ako ku Taiwan and China for fake degrees, athandize alimi a fodya.

james
8 years ago

Njira ya bwino alimi azigulitu zipangizo nthawi yomweyo akugulitsa fodyayo.

Kennedy nali
Kennedy nali
8 years ago

Chamba, mukukhumba kubela walimi eti? Kweni vyiru ku malawi kwali ine. Chiuta wamulangeni nakuba kwinu.

chinkombaleza gumanyundo gowa
chinkombaleza gumanyundo gowa
8 years ago

A malawi ena ndi obvuta. Kuti Kwacha igwe ayambanso ndi iwowo kudandaula chabwino ndi chiti? Mukufuna President atani. Anzanu tikukondwera kwacha ikamamera mizu.

malawiana
malawiana
8 years ago

We have been hearing this story of diversification for ages now and no progress on the cards. Reason is that the government departments responsible are technically dead with no vision. Agriculture extension services are dead, departments of SMEs and Industry at Ministry of Trade died long time ago. So who is going to champion this diversification? The President?

point blank
8 years ago

It looks like Malawians are beginning to get back to their senses or the noise makers were a political party sect. I remember during the same period last year all insults went to the President. But today people are making reasonable comments if they’re not being partisan. Learn to understand dynamics of trade.

soko
soko
8 years ago

chaka china alimife tidzangopangane osalima fodya. Tidzavutika koma boma lidzagwa. Aliyense amene akufuna kugula katundu kunja nyengo yake ndiino alimi osauka omwe alima fodya zaka 20 koma alibe ngakhale nyumba abweretsa dollar yotchipa. U can fool people some of the time, not always

Mchikumbe #5
Mchikumbe #5
8 years ago

The problem in Malawi is that we have a Tobacco ControLLED Commission not a Tobacco ControL Commission!

Read previous post:
First Lady says Malawi children are battlefield in war to contain HIV/AIDS

The First Lady of the Republic of Malawi, Madame Gertrude Mutharika on Friday called upon parents in the country to...

Close