Email a copy of 'Two Mozambicans arrested over human bones' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

39 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MAMAMIA
MAMAMIA
8 years ago

alangidwe basi

Douglas
8 years ago

apolisi timadalira inu amenewo chitani nawo basi.

shaaaa!
shaaaa!
8 years ago

paja alomwe ufiti nde wao.ndi ncthito yapakhomo pa munthu yomwe,mpaka atchulepo juju.
mafupa aawanthu saona za chilendo.zikasokonekera mukazipeza ku leba office kokasaka ntchito,anthu osasamba.

Apolice chitani nawoni ampala bwazi onsewa.tatopa ndikumva nkhani zaku manda.kkkkkkkkkkkkkkkk

STEVIE THUMULA
STEVIE THUMULA
8 years ago

Aphedwe aku Mozambiquewo.

syamboza
syamboza
8 years ago

thy killed a person they need t killed also. They removed someone’s flesh remove theirs too

Vaanwyk ku Mzuzu
Vaanwyk ku Mzuzu
8 years ago

yemwe amamugulisayo afunsidwe bwino. mwina inali deal ndie wangowapachika anzakeo poti anadulisa mafupawo. munthu sangango bwela kwa ine kut ndimugule mango pomwe ine sindidya mangowo. no smoke without fire.

k.laston
k.laston
8 years ago

anthu oipa awa alandile chilango chokhwima kuti wena atengelepo phunzilo chifukwa cha khalidwe loipali.kufuna kulemela mu njira yoipa ya chidule .kuchitabwino sathamangila ai anthu opepela lero dzawavuta.

iv

ankhoma
ankhoma
8 years ago

look at them. stupit.

lawrent malongo
lawrent malongo
8 years ago

It need to give them life in prison,anthuwa ndiwoipa osamawanyengelera.zilango zikumakhala zophweka ndichifukwa chake sakuleka moyo oipawu.

chidumayo
chidumayo
8 years ago

Last time a group of human bones sellers from Mozambique were given a bell of k20,000.00. This indicates that its not a serious offence. Can we revisit our laws. Shitiiiiiiiiiiiiiii Nyasaland laws.

Read previous post:
Malawi Carlsberg Cup re-launched, 2015 format unveiled: Eight top teams to be seeded

Carlsberg Malawi has given Football Association of Malawi a boost after announcing that it will sponsor the cup this year...

Close