Email a copy of 'Two students from same family drown in Balaka' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Two students from same family drown in Balaka' to a friend
Malawi Minister of Natural Resource Energy and Mines Atupele Muluzi has leapt to the defence local non-government organisations (NGOs) and...
SAD NEWS + R I P +
Iwe Mtumiki! Ndiwe mtumiki wa demoni. Ndiwe satanist!
Kodi mukamati rest in peace mumatanthauza chani!kusowa zonena?mumauza ndani kt rest in peace?ofawo amakumvani?mungapangise munthu kt ause mumtendere inuyo-mumawerenga bible koma?
Be civilized my friend
May their soul RIP
Khani yonvesa chisoni iyi,R.I.P
Zonse mwiniwake ndi ambuye ndiamene amaziwa nthawi ndi nyengo
Aaah pepani ndithu tafa tonse pepani,RIP koma mvulayinso eish pepani.
May they Rest in Peace.Its shocking to loose 2 children at once.
I’m sorry its sad news,R I P
Pepani ndithu mai wa ana. Mumawakonela tsogolo ana anu. Mulungu wathu akutonthozeni. Pepani.
Makolo, aphunzisi, a police, ma councilor, mafumu, a mabungwe, chonde tiyeni tilimbikise kuwaphunzisa ana zoyenela kuchita mvula ikamagwa.