Ine ndinakumana ndi ngoziyi ca ma 10 koloko utsiku bt it was painful to see 4 people died in same spot including a child less than 5 years in this accident. Pliz follow the rules mukamayendesa galimoto moyo ndiwofunika chonde. Only GOD ALMIGHTY KNOWS THEM THAN US
A Konyani
9 years ago
The driver’s identity,although am not 100% sure,must be John Chigumula of Tchete village T/A Mwambo, Zomba. MAY THE SOULS OF THE DEPARTED REST IN PEACE.Koma msewu wathu wa Zomba-Jali,wafika pokaikitsa.Almost every week kukuchitika ngozi.Previously,it was at Lomoni,Mamphanda @ talking about accidents involving cyclists,motor cyclists & pedestrians,they are countless.Should the blame be shouldered by the police?,road users?,or there is satanic intervention? May the good lord have mercy on the innocents who are losing lives eg the just demised six-yr old.
Rest in peace.
Mukuonatu munthu kuzembera mkazi wake ndi kukafa pa ngozi ndi chibwezi. Very shame anthu osewa ndikuwadziwa. Mkaziyo ndiwaku Zomba koma amunawo ndi akuno ku Salima ndipo amapita ku chikwati. Mkaziwo ndi chibwezi cha driver yo. Mwana yo ndi wa Driver yo. Pochoka kuno anali ataledzela Mowa. galimoto yo ndiyobweleka.
phil
9 years ago
stella its frm zomba en she woz commonly found @ a drinkn club HIHG FIELD In Zomba may hr soul rest in peace she woz beultful

RIP
RIP
RIP
RIP
how about the drivers licence for id?