Email a copy of 'Village headman arrested for chopping man’s private parts – Malawi Police' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Village headman arrested for chopping man’s private parts – Malawi Police' to a friend
Legatum Institute's 2014 Prosperity Index puts Malawi 118th globally Malawi has dropped 12 places in the 2014 Legatum Prosperity Index, which...
Mafumu Kufuna Kulemela Kumeneko
Let that village headman be hanged!
signs of the time Bible linalemba kale tsoka okwanilitsa malemba
koma abale signs of the time owerenga khala maso
Amalawi mwatani kodi? mwayiwala chikhalidwe chathu mwayanja zachilendo.
okumwa mowa musamale chifukwa nzanu akati ndikakumwetsa osangopita kumowako ndi kamwa lomwera mowalo kapena chimimba chokhuthulira mowacho ayii ayi! kumapita diso lili wide open,I mean be able to sense the situation and location as well as time.
Waipempha death sentence
Munthu akuopsa kuposa nkango, akuyamba ndi mafumu, malo ogona tizikapempha kwa ndani kukatidera? Popeza amati pita kwa amfumu akatichose ziwalo zobisika, plz judge death sentece to that absord chief.
IF I WERE AJUDGE NDIKANANGOWAPATSA DEATH SENTENCE
Why are these photographs posted? Why does the suspect have the evidence to show others? This is bizarre and disturbing on many levels. (I see, sensibly, that the photos have been taken down and the one posted cropped to hide the ‘evidence’.)