Email a copy of 'Violence at Kabudula's burial as Chief Lundu censors MCP' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

30 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mtete
7 years ago

Is Lundu ever sober? How did M’mang’anja find himself deep in Chewaland? Here is another comedian trying to please another clueless comedian. Koma ndiye mwatifwala inu a Lhomwe ndi a Mang’anja. Bola A Yawo Ulemu alinawo. Shàaaa!!!!

DODODO
DODODO
7 years ago

ZOONA

DODODO
DODODO
7 years ago

MCP KUDZALAMURA NDE AYI….LUNDU IZO NDI ZOONA

Namalira
Namalira
7 years ago

Ha!!, Ha!!. Ha!!, Kodi iwe mfumu ya a Mang’anja zoona wakhuta mitu ya njoka ndi mphenembe ndiye kumakalalata pa maliliro a pa khomo lo Chewa. Kodi ngati uli mfumudi yozindikiridwa ndi mfumu Ngawaundi ukanalankhula zopusazo pamaliro?. Apa mafumu onse o Chewa mukhale pansi kusankha mfumu ya Chichewa osati awa otumindwa ndi Milakho ya Lwomwewa ai. Dziwani kuti wanthu omenewa ofuna kusokoneza khalidwe ndi miyambo yathu. Ku Central sankhani mfumu yokhazikika osati gulu la timafumu ta ku Kasungu timene moyo wawo ungofuna kudya kutaya chikhalidwe cho chewa. Pamaliro simalo opangira ndale za Chilomwe kapena za amang’anja ai. Nkhaniyi iyi ifunika ipite… Read more »

statesman
7 years ago

Iwe ukuti major pen ndwe galu etii!! Ndwe chitsiru,mbuli,kupusaa! MCP yazuza mafumu ake otiwo apa,ukunena chikutumbwe cha mfumucho called Lunduu,kkkkkk to hell with him..ngati nkhaniyi yakuvutani kunvaa pot ndichingerezi mudakangokhala osapanga comment.we the chewa maliro timawalemekeza,ndye ichocho ndi nkhope ngati nkhumbayo ndikumakayankhula manyi pa maliro? Azipanga zimenezo kwawo konko,mmmxiiiew ,that’s y even anthu akwao sakychifuna chimunthu chimenechi.all this because of stupid chiefs like Kaomba and Lukwa..zitsiru za mafumu..

Mwaiwazama
Mwaiwazama
7 years ago

I have said several times about Lundu. Lundu is not Chewa but a Mang’anja why do Chewa chiefs align with him. See what he does now. All this mess is because of Lukwa, Kaomba, Dambe (MC) and Nthondo because of greed. Chewa chiefs your greatness is deteriorating. Look at other chiefs even among the Mang’anja. And why is Gawa silent on traitors? The Chewas are disengaged in many areas and yet their chiefs are having fun with DPP

Bazzoka
Bazzoka
7 years ago

Lundu ndi mfumu yamadyera mphontho ndi yopepera.

Achi
Achi
7 years ago

In all fairness chief Lundu errored. Why bring politics pa maliro?
Everyone knows that Lundu has access to MBC where he could pour out his heart in line with the desires of his political masters and political inclination.
It was a great insult to the chewas.
A Lundu mumapitako kukalira mfumu nzanu kapena kukachongetsa kwa mwini chikwama? That was bad

Lundu
7 years ago

CHINDERE CHAKUFIKAPO CHA MAFUMU ONSE DZIKO LA NYASALAND

Imbwa
Imbwa
7 years ago

Galu wamfumu Lundu. Kochewa timati tiona phwetekere akapsya. Munthu sungamunyozere pakhomo pake chifukwa choti kwabwera mlendo wachuma. Achewa sitilola zimenezo ndife ozindikila osamatitengera kumtoso ngati nyama yagalu. Galu mnzanuyo m’dyereni koma ife ndi MCP basi

Read previous post:
Catholic Church marks Ash Wednesday, start of Lent

Catholics in Malawi and around the world trooped to churches on Ash Wednesday, marking the beginning of the 40-day Lenten...

Close