Email a copy of 'Violence resurfaces at Kamuzu Stadium: Surestream frustrate Red Lions in Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Violence resurfaces at Kamuzu Stadium: Surestream frustrate Red Lions in Malawi TNM Super League' to a friend
Mzuzu University (Mzuni) FC continued its superb form to beat Moyale 3-2 in an entertaining Mzuzu city derby in TNM...
Asilikali amazimva alandire chilango amenewo
Ref oyipa ofunika asazaimbilenso mmoyo mwake,
Soldires should start their own league and play against each other and beat each other
zanyanya
The referee was incompetent and needs to be disciplened. He was the reason behind the ugly scenes. Let us not allow this to continue denting the image of our beloved sport.
Ma Reds sanalakwe. Ref uja ndi wa fodya osatha kuimbira mpira. Akangoyamba kugulitsa nthochi. I hate the funs who stoned Red Lions’ bus.
Muthokoze anzanu apa chichiri camp !!ndiye muzapangeso mukazakumana ndiife mzika tizaocha coaster.
TIKUFUNA CHIGAMULO MWACHANGU, AMENE ANAMENYA REFEREE ANOONEKERATU PAMENE PAJA, NDIPO SULEMANI ANALI KONKO.ikanakhala , NOMA, BULLETS kapena SILVER lero lomwe chigamulo chikanapelekedwa dzuwa lisanalowe. zimandiwawatu ine.
expect this with surestream.Timuyi imagula ma referee nyatwa ndiye simunati muona ma game enao
Iiiiii!!! Napepe malawi kuzambiyaku taluza nkhano zake ndizomwezi basi